
Duwa Lyrics
- Genre:Others
- Year of Release:2023
Lyrics
Duwa - Eli Njuchi
...
Fumbimbi! Go check go check go check go check go check go check go check
Njuchi!
Duwa×2
Njuchi apeza duwa duwa aaah ahyi!
duwa duwa aah ahyi!×2
Eh yeah!
Amakambirana Njuchi ndi mkazi wake amakhalana mmmh!
Amalozerana Njuchi ndi duwa lake zimanvana mmmh!
Nthawi ya mvula, duwa langa limawala!
Zikati zilibwino, duwa langa limanunkhira iwee!
Hook......
Verse 2
Koma duwa langali likati lidemande
Duwa langali ndikati ndithilire eh
Limayamba kufota ngati mthumba musali bho! oh uwooh!
Limamera minga ndikangoti ndilibe money (money, money)
Ndimakamamidza machedza, majokes anga ndimaseka ndekha mmh!
Or ngakhale ku praiza, Sunday ku temple ndimavaya ndekha
Sanva zanzake eh(muli makanimakani makanimakani)
Koma salary ikangolowa! (maphone maphone maphone)
Hook