![Nyimbo Za Mtima](https://source.boomplaymusic.com/group10/M00/07/25/7500125c545c43e3808718caa0adec6a_464_464.jpg)
Nyimbo Za Mtima Lyrics
- Genre:Afrobeat
- Year of Release:2022
Lyrics
Nyimbo Za Mtima - Lawi
...
Pamene ndasauka ndalemedwa mtima Bwenzi langa, limba langa limbitse mtima Pamene ndasauka ndalemedwa mtima Limba langa bwenzi langa limodzi mtima Yimba nyimbo, nyimbo ndi mtima wa chiyembekezo Timayimba nyimbo, nyimbo mpaka mtima utapepuka Timayimba nyimbo, nyimbo ndi mtima wa chiyembekezo Timayimba nyimbo, nyimbo mpaka mtima utapepukanso