
Sangandilengere Lyrics
- Genre:Afrobeat
- Year of Release:2022
Lyrics
Sangandilengere - Lawi
...
sangandilengere wina omvana nane sangandilengere wina..
sangatsegule khomo la kumwamba kudzandilengera wina
sangandilengere wina okondana nane sangandilengere wina sangatsegule khomo la ku Eden kudzandilengera wina poti analenga iwe,iwe!iwe,iwe!poti analenga iweyo,iwe,iweyo ×2
mtima wanga umagunda ndikalingalira iweee ooh
monga kumwamba anati tikondane ndakukonda iwe
pondilenga anati ondithandizira uja ndiwe
nthiti yanga ija ndiwe
sizoswelananso mitima mpaka kubwalo zachibwana ine sindipanga nawo poti chauta pokupanga anakonza extra ordinary ndipo anatseka factory oooh na na na na sangandilengere wina ofanana nawe sangandilengere wina sangatsegule khomo la kumwamba kudzandilengera wina bwenzi langa lomvetsetsa sangandilengere wina ×2
sangatsegule khomo la ku Eden kudzandilengera wina
sangandilengere wina omvana nane sangandilengere wina sangatsegule khomo la kumwamba kudzandilengera wina
sangandilengere wina okondana nane sangandilengere wina sangatsegule khomo la ku Eden kudzandilengera wina poti analenga iwe iwe iwe poti analenga iwe iwe iweyo ×2