Inu Ndi Abale Anu Lyrics
- Genre:Afrobeat
- Year of Release:2022
Lyrics
Inu Ndi Abale Anu - Lawi
...
Moto m'dambo, fire in the jungle
Somebody please put out the fire
Akayiwala munthu njira zake amphunzitsa ndi galu
Moto m'dambo, kalanga nchilango
Somebody please put out the fire
Pamudzi pa umunthu payaka moto
Ndati ndikukumbutseni, moyo nkang'oma
Ukhala nulira, oyimba ndi wena
Kuchezera mphechepeche mwa owamba zikopa
Wosamanga milatho, amadumpha dzidikha
Moyo wa chule ndi mzake tsokonombwe
Sungati bwanawe tiye tiwongole miyendo
Ali nako ka nkhani alibe chibale
Inu ndi abale anu mdzikhala pa bwalo
Inu ndi abale anu, ndinu mbambande kuposa golide