Get Premium

Musawalange Lyrics
- Genre:Afrobeat
- Year of Release:2022
Lyrics
Musawalange - Lawi
...
Musawalange ondilakwira mukhuluke njira zawo (musawalange) Wo oh oh oh Musawalange iyayi Musawalange ondilakwira mukhuluke njira zawo (musawalange) Wo oh oh oh Musawalange iyayi Muli ndi chifundo mumakhululuka Mundikhululukirenso ine ndemwe Chilungamo changa chili ngati sanza Mukupupuluma ndikukwiyitsani Ndikukumbutsani mtanda Ambuye wa chifundo pungulirani chiyero mwa ine Ondilakwirawa muwapatse chikumbumtima ndi chikondi Ndi kuwalemba mu buku la moyo (musawalange)