Loading...

Download
  • Genre:Afrobeat
  • Year of Release:2022

Lyrics

Amanje - Lawi

...

Akugwa anatchona mu Sozibele

Ataponya maso pa Jatibe

Anaiwala za ku Nyasaland

Akomedwa ndi anyezi ndi mavembe

Ngakhale moyo ukusintha

Atchona sakubwerabe

Tinamva akuwathamangitsa

Ali chitchonere sakubwerabe

Amanje, Amanje

Kodi mudzabwera liti Amanje?

Amanje, Amanje

M'mudzi mudzabwera liti Amanje?

Amanje, Amanje

Kodi mudzabwera liti amanje?

Amanje, Amanje

Mthengo, mudalaka njoka m'thengomo

Tidakumba bawo pakhomo paja

Pansi pa mtengo wa mango

Timakhalira maso kunjira

Tingalandire alendo

Asanduka chigawenga

Kabwerebwere ku ndende

Koma kwa ini kulibe mkuwe

Cha kwanu leka

Amanje, Amanje

Amanje, Amanje

Kodi mudzabwera liti Amanje?

Amanje, Amanje

M'mudzi mudzabwera liti Amanje?

Amanje, Amanje

Kodi mudzabwera liti amanje?

Amanje, Amanje

Mthengo, mudalaka njoka m'thengomo

Kwanu mkwanu nkhale pa bwinja

Tsiku lina muzakusowa

Tikudziwa muli ndi luso la utelala

Koma musathere moyenda

Tinamva anasintha dzina

Ukamberembere adakachitabe

Ngakhale moyo ukusintha

Ali chigonthere sakumverabe

Amanje, Amanje

Kodi mudzabwera liti Amanje?

Amanje, Amanje

M'mudzi mudzabwera liti Amanje?

Amanje, Amanje

Kodi mudzabwera liti amanje?

Amanje, Amanje

Mthengo, mudalaka njoka m'thengomo

Similar Songs

+

      -   or   -

      -   or   -

      NG +234
          -You can log in via below methods-
          Reset password via e-mail
          -or-
          Reset password via e-mail
          If you have any questions, please feedback on Boomplay App or send an email to [email protected].

          Please Select A Playlist

          Add New Playlist

          Share on

          Embed: Love & Light EP

          Custom Size :

          • Default
          • Desktop(300*600)
          • Mobile(300*250)

          Type :

          • HTML/HTML5 (WordPress Supported)
          Get Boomplay Premium
          for
          Payment Method
          Pay With
            Review and pay
            Order Date
            Payment Method
            Due Today
            Flutterwave
              Subscription Successful

              Congratulations! You have successfully activated Boomplay 1 Month Premium.

              Now you have access to all the features of Boomplay App.
              Payment Failed

              Please check your balance and then try again.

              You'll lose your subscription if we don't have a working payment method for your account, so please check your payment details.
              Need help? Contact Boomplay Subscription Support.
              Payment Processing...
              10 s

              Payment is being processed by . Please wait while the order is being comfirmed.

              Payment Processing
              Your order is processing, and it may take up to a few days for the service provider to handle your payment. Please kindly stay tuned and check your order status in ‘User Center’.
              About Order Status