
Tokota Lyrics
- Genre:Hip Hop & Rap
- Year of Release:2022
Lyrics
TOKOTA
Majealousy (YA) Majealousy (YA) Majealousy (YA-YA)
I dedicate this one to all the haters
I pull up with my day 1 nigga- TANA!
This 1 is for everybody that be talking negative ndinu makape-
HOOK
Inuyo mumango-
Tokota Tokota Tokota Tokota Tokota Tokota Tokota Tokota Tokota Tokota Tokota ndinuma-KAPE!
iFEYo tikumango-
Songa Songa Songa Soma Soma Soma Songa Songa Songa Soma Soma Soma Songa Songa Tsogola Tsogola-BELE!
VERSE
AAngolubwa ngati Nyau King amveke ndinatha
Ndabwela ndima punch-line ma kicki ngati shau-lin Master
Sindimalemba nnakuuzani kale
makape mukuti mwandiyiwala-eti
ndabwela ndika reminder you MCs aint amazing ndinu mbale/
zi stylo zomenya ma hip hop a crazy wa tinayamba ndife mwamva- nkhale mu disse!
simungafikile malevulo angawa nnachokela straighty ku mwamba
mafana mukuchepa kaba mulibe luso mulibenso ndalama- busy ku!
tokota ku hater madokota mukanyumba kanu ka malata
timanyimbo tanu ndimango skippa
nchito kulalata kujaja zinthu zomwe anzao akupanga
nyengo za sintha mpwanga
tikucheka zama ninja panga
HOOK
uKAmango-
Tokota Tokota Tokota Tokota Tokota Tokota Tokota Tokota Tokota Tokota Tokota ndiwe-KAPE!
Uwona chimbenene Phwanga Uwona chimbenene
Usamango lubwa lubwa akudula lilime
Uwona chimbenene Phwanga Uwona chimbenene
Usamango lubwa lubwa akudula lilime
Iwe Kape!!!
VERSE 2
oSamango tokota tokota kumawona kaye mukukambisana ndi ndani
Nyimbo zanga zanyuwani zimunazimve zonse mwayambapo kale chidani
dolo amane mukumamu praiser yo kwaineyo iyeyo ndi fani
real nigga pay respect to the veteran kapena ndikuu-wonese chi phazi
mafana amasiku ano your funny
So U got views izonzako
dola bills izinzako
round here we aint amused ndi music yako
ndala akachoka
mafana amatasaaa
kumavala boxer wanga eti nkusandusa trouser
Ine si size yanu mafana nonse pelekani- ulemuuuu
pa sit yanga muchoke mwachete chete ndisanakupangeni shame-uuu
sheguuu kapena ukufuna 'kuchitise manyasi pa gulu pa- sunagule malo mwana mano aja naakusungisa aja
ndikugulula
ine ndi king aise i came for my crown
ya ya ya!
AM the day after graduation day zabwezeni gown
rap university tana ndi chancellor
WATch Ur mouth
HOOK
Osamango
Tokota Tokota Tokota Tokota Tokota Tokota Tokota Tokota ndiwe-KAPE!
busy ku
mabula mabula mabula mabula mabula mabula mabula mabula mabula ndife ayinIe-AKE!