Loading...

Download
  • Genre:Hip Hop & Rap
  • Year of Release:2022

Lyrics

JAN DON'T WORRY

January amebwela ndimavuto ake.

We on the grind

Kila siku mina saka adi ni pate.

Ka gwa gwa gwaaa

( eh )

January amebwela ndi ma vuto ake eh

We on the grind

Ngati ndili ndi ndalama zako sinayiwaleee

Nzakupasaaa

Vuto sine koma ndimuthumba mwangamu

Everysingle day we tryna solve another problem

To all my hustlers tryna pay your landlords lets keep on grinding grinding till we get the doh

Wah


Ehhh

Mundiloleee

abrazi ndibwelekeniko kangongoleee

A banki teller nuuu

3 weeks mundipaseee

Ndizakubwezelaninso ndika interest


Ndingofuna ndiguleko ka chokudya (ah)

Mayeso ayandikila nkusowa school fees eh

Ndi January busymess ikuvutaaa

nchito Salale sanatilipileee ey


A banki manager ndithandizenikon

Mundilole nditengeko ka loan

Ndikudziwa inaija sinabwezeee

Chonde ndimveleni chisoni

Ndikudziwa mufuna collateral (collateral)

Nyumba ndiiyo (nyumba ndiyo)

galimotonso (galimotonso)

Bola khobili ndikodyetsako moyo wo

Tisafe ndijala Mungo panga choncho (Cho)

zinthu zapa dziko izi

tizazisiya konkuno I wasn't born rich...

Bola ndingopezako ka peace

Nthima sulimmalo gata provide for my family ih ih


CHORUS

Anapanga system ya ndalama ndichitsilu kwambiliiii (kwa mbili)

Bola bata trade ijaaaa

Bola bata trade ijaaaa

Nthawi yachimake dzana sitimalila zambiliiii

Nyumba madzi ndi nsimaaa

Nyumba madzi ndi nsimaaa


VERSE

Ya!

I been inside! /I gata grind / I gata letget me the gwa (gwa)

Talking to God/ gime the gwala / my njale ikufunika gassss

Hustling getting paper from my guys

Sintimakonda kupanga chibwana pa nkhani ya business

Gata make a living we be looking for the cash

Eversince I was a little kid

Mama told me get your dividends

Daddy told me get an education

Usalive life imene tilifee

Struggling tryna make a better means

Sacrificing every single cent

Amatenga ma loan praying every morning tikhale moyo wabwino pa tsiku men

& when the going got rough

They never give up they working so tidious

Switching jobs every month

The food on the table delicious incredients

Mummy amandisamalila bwino ineyo ndima 2 sisters

Daddy amatiyan'ganila kutiphemphelela kamfunse francis lawi cousin

Banja la Zuze lo dalitsika

Tadusa muzinthu zambili mavuto achuma kusausika

Kunditumiza kunja kuti ndikaphunzile koma sindimauzika

Ntazindikila naayamba ku worker hardi pano zinthu za sintha

Uphawi uja watha situation ili bho

Ndayamba kupeza ka doh

In the name of the lord am growing my platform

We be selling all my songs

Uku ndi uku apo ndi apo

Posachedwapa ndikhala katu source

Boss hustle zimaatha tikupaka improve

Kupusha ka ngori

Huh _ya

But I remember ndiku zemba angongole

Angogoleeee

Ndikazipeza kugula mphasha ndikongole

Ndikongoleee

Skulu ikuyenda anthu andi sponse

Sponseee

Kuyamika namalenga muzinthu zonse

zinthu zonseee


CHORUS

+

      -   or   -

      -   or   -

      NG +234

          Please Select A Playlist

          Add New Playlist

          Share on

          Embed: Love & Light EP

          Custom Size :

          • Default
          • Desktop(300*600)
          • Mobile(300*250)

          Type :

          • HTML/HTML5 (WordPress Supported)
          Get Boomplay Premium
          for
          Payment Method
          Pay With
            Review and pay
            Order Date
            Payment Method
            Due Today
            Flutterwave
              Subscription Successful

              Congratulations! You have successfully activated Boomplay 1 Month Premium.

              Now you have access to all the features of Boomplay App.
              Payment Failed

              Please check your balance and then try again.

              You'll lose your subscription if we don't have a working payment method for your account, so please check your payment details.
              Need help? Contact Boomplay Subscription Support.
              Payment Processing...
              10 s

              Payment is being processed by . Please wait while the order is being comfirmed.

              Payment Processing
              Your order is processing, and it may take up to a few days for the service provider to handle your payment. Please kindly stay tuned and check your order status in ‘User Center’.
              About Order Status