Panjapa Lyrics
- Genre:Hip Hop & Rap
- Year of Release:2022
Lyrics
PANJAPA
boom! boom! ya ya.....
HOOK
Panjapa YA
Panjapa YA
Tikumane panjapa YA
Panjapa YA
Tikumane panjapa YA
Tikumane panjapa YA
Tikumane panjapa YA
Tikumane panjapa YA! (PHU BOOM PHOOM!) Huh
Verse
Kodi mani panja munkati chani tiwonetsana panjapa
tikangoyiyambitsa nkati munomo tiswanyamo ma tambula
man....paja tsikulija munati chan
eh mwayiwala....ndikukumbutsan
MBHAMA!
ndimadana ndi mafana otokota zinthu zo pusa wamva!
EEE mani tayimani please choosy kaye
simesa amayamba ndikupanga warning'ngi?
ine ndilibe za 2'coloko!
Tikambilane panjapa
Tikambilane panjapa
Ndikaledzela ndimakamba zinthu zambili chonde mani ndikumane panjapa
Oouu Weee!
Sitimavana bwino nkatimuja ndikudziwa mukufuna katumba kanukaja ndikupatsani
Next week!
ukalakwa kumadziwa kunamaaa
akakutulukila dziwa kuthamanga osalimbana ndima gambaaa
bwana businesi sitikamba tikayaka tikumane pa mawaaa
iwe nkhani zakubala ndi sikileti osakawuza ababaaa!!!
Eh!
sunday kuchalichi kokalapa timaphemphela (HALELUYAH!)
mbale ya offering ikafika apa timapeleka ( ya ya ya )
buda mina saka malawi goldi niaje bazenga
(mannn!)
Chamba changa chi ndi changa changa osayesa ndapenga
(prrrrrrripidhdhhh!)
kuchoka-pa kenya-pa zizikuyenda-ka mutu wayima ndakhala-pa chenga-pa ukancheka ndiku chaser ka paper-ka osandiwawisa nditha
ku-ku-kugendaaa!
SEMI-HOOK
chapanjapa
tigendana panjapa yEH yEh yeh
paja mani munkati cha?
nnaledzela tsiku limenelija mani tithokane panjapa
chapanjapa
lelo tithana chapanjapa
tsiku lijali muna bisala nkatimo lelo tigendana chapanjapa
Verse 2
Muno mwadzadza fansi heavey moti mulibe ka space eh
ndilipanjapa
mukandifuna mukudziwa komwe mungadipeze
eh ndilipajapa
chapa fupi ndipa windo kusaka ka fresh air
Eh
eti kakundilondola ngati seazoni ya mango ndi njenche
olo ntakwela ndege mumuwuze kondakitala andibwezeleko chenge
tssss!
chapanjapa tingoyasa ka nazika mwantendele
paja zogulugusha inetu ndinasiya!-palibe ndingatenge
zanga ndi paintsi bluntsi- machule ankandifuna kwa pasa teche
Eh
phazi ndithandize
Eh
Pauchi Josephy
fanzi kuthokota konkordi yachina tana e-teleeeh!!!!!
kandala ko kongola chilembwe
chi jomo mu thalawuza chili mbwe-EH!
chi chani chimenecho ukachi cheka chapanjapo chitango khala phe!!!!!
HOOK
Panjapa YA
Panjapa YA
Tikumane panjapa YA
Panjapa YA
Tikumane panjapa YA
TikHumane panjapa YA
Tikumane panjapa YA
TikHomane panjapa YA! (PHU BOOM PHOOM!) Huh