Mwanawamkachisi Lyrics
- Genre:Hip Hop & Rap
- Year of Release:2022
Lyrics
MWANAWAMKACHISI
Mwanawamkachisi
Amadya zokudya zamkachisi
Tana x2
Mwanawamkachisi
Amadya zokudya zamkachisi
Eh
Mwanawamkachisi
Amadya zokudya zamkachisi
Ma fruits ma nachesi can't u see how we lit!
Machesi
Eh
Mwanawamkachisi
Amadya zokudya zamkachisi
Mwanawamkachisi
Amadya zokudya zamkachisi
Eh
Mwanawamkachisi
Amadya zokudya zamkachisi
Ma fruits ma nachesi can't u see how we lit!
Machesi
Uh
VERSE
Mwanawamkachisi amadya zokudya zamkachisi
(Eh)
Zikamuvuta ntumba amazapisa mbale yaza offering
(okubayooo)
Ma fruits ma nachesi kumapisa koma mwathayimini
Eh
Olo agalu amadya zosalila za ana aku palace
Tsss
Kublowa zijazi zakamuzu banda ndagula ka chalice
Nane nkufuna ndikumane ndi most high ngati mosesi
Ku burna bush ngati George Obama ndikaleko wize (Ya)
Chonde musandipangetu report ngodi wangayu si white
Malemba analemba mwana wakachisi azadyanso zamkachisi (keche!)
Kuthawa kachimfine ka Korona ndazibisa mu handkerchiefiii (cheche!)
Hachu!!! I am so blessed ndikahetsemula ndima profiti ndilimu bush!
kuzithandisa kuchile kusaka miracle khobilis
Whoo!
CHORUS
Mwanawamkachisi amadya zokudya zamkachisi
Mwanawamkachisi amadya zokudya zamkachisi
Mwanawamkachisi amadya zokudya zamkachisi
Eh ma fruits ma nachesi (ye we so lit!)
Can't u see
Fire!
All my chains made from sapphire!
Fina crush the internet like a virus
I been waiting way too long praying to the son spirit & the father Aya sireh!
Western union let them numbers get wired
Holy communion preaching to the choir
We gidigi gidigi it kwagmire
Hahaha
VERSE
Ine ndi John
U can't see me
Kamfunse John! U can't see me
U is a funny dude! Kamsime we be dropping the doh! siahamsini
nkazapanga show! come see me with 1 million pa door
Ah siiine _yanga ija/ so expensive
ka shillings
Ulipa top! ka ceiling
Tizakudroppani pansibe/ mafana mulishallow kachinsime me am kilimanjaro to river shire /
That means am high! simganditsitse/
Kodi iwe bwanji? Sinampuzile /
Zoti ndiwe bwana sinaziziwe /
Pwanga ndi we mwana sungandipusise
Ine ndi biggy plus makaveli /
Working hardi sleeping very late / wake up early
Iwe ukudya zamkachisi ngati Ana a Eli
Ine ndima panga zanga daily
Mwana wa Pastor! major 10
Ine ndi master!
caputain drunken master ngonelo ndithakumwa ma cupu 10
Vinyoyo- nyimbo zanga ndima freestylo
Sindilemba ndi Bicky peni
Ma iPhone ma silly celly
Nkutokha mo nkota nkota suli straight
Ntapota nkhobatu nduusutiseni
Ukatola ka dola ndi sungise ine ka starleti kangakokhako ndisunthileni shati versace ndi sitileni neighbor jealousy nsanje ndi silileni nkazi wanga wa better yo ndi siileni kanjale ko bweleka
Ndiswitche lane ma rapa muli sicki nduuchiliseni
Nkubayilani ka drippy nduushirinjeni... Shirinkeni
A dootolo adolo obwata abwela nkuchiliseni
Mumayesa ndinu otenthaa et
Malo anga muna tenga et ma middle mani Kumangodya ma tender et
Munajichocha naka 10 K eti
Tsono ndabwela kudza tenga katumba kanga kaja kantedza
Ubweza zonse zizamatheka ukutipfweee wakumana ndi undertaker eh
Mwanya wamkachisi Amadya zokudya zamkachisi iiii
Adaawa ndachitsilu amabisala nkati mwa chalichiii
Lelo awona Chinameta nkhanga mpala ndabwela mmaknifeee
Amazemba chokwawa Lelo wakumana ndikwangwa pa nsana osampasa ntaji menye ni axeee
CHORUS