Umve Lyrics
- Genre:Hip Hop & Rap
- Year of Release:2022
Lyrics
UMVE
Mwayamba umve
Mwayamba umve (ya)
Mwayamba umve
Mwayamba umve (wear your mask)
Mwayamba umve (eeeh)
Mwayamba umve (eyyy)
Mwayamba umve (eh)
Mwamba Eh ehh ehhhhh!!!!
CHORUS
Mwayamba umve (nyasi)
Mwayamba umveti (kha phuu!)
Mwayamba umveti
Mukudya thukuta la anthu osauka
(Mukubaaa)
Masuku pamutu eti (mukuba)
Masuku pamutu eti (mukuba)
Mukumafuna katundu wanthu anzanukaaa
Mwayamba uhuleti (akazi waa)
Mwayamba uhuleti (mamaniwaa)
Mwayamba uhuleti (saankaziwa)
Nditalikileni social distance
Verse
Mwayima pa gulueti ahhhh
Kukwela pa chulu eti ahhhh
Kufufuma ngati ka chule eti kuzipopa ngati ka chubu eti ahhh
Machukuchuku eti
Kuzifila ngati juice eti
Kungopeza ka million mwayamba Kuzifila ngati ndinu a bill gates
Mababy mwaphula kanzungu eti
Chamu nzanzi mu ku chaser ka chuma eti
Kuziphoda nkhope ngati gule eti
Powder la mbina kuyi chuna eti
Too late// tsogolo lanu lilikumbuyo eti
Ur futures behind kuyi booster ngati bulleti
Kick ki bridgeti wayamba uhuleti
Ma mani wanso ndima gay eti akukulisa mbina ndima buledi
Kumyata myata pa towni pa eti kuhasa mpaka kugula benzi ah- nkhalidwe lanu lonunkha
Umveti nkhutukumveti
a teacher la alugona nima pyupyulu (pupil) kumakisa skulu graduate
Omunawa nzipwelekete muzipwetekeko ukuku kukhale weti
Mulikugundika kudya ma puleni puleni ngati ndinu ampala buteteti
Mwayamba umve chonsecho munamala koma simumakhuta eti
chimkhalamba zaka zake Zaa akazi ake! sakufuna koma zaana asanakule eti
Chimimba khuli ngati khumba eti
Chonsecho ndi bwana wamkulueti
Salale kutha Kuma blangeti
Mukufa mukamwa chokumwa ichi zopusa izi...
CHORUS
Mwayamba umve (nyasi)
Mwayamba umveti (kha phuu!)
Mwayamba umveti
Mukudya thukuta la anthu osauka
(Mukubaaa)
Masuku pamutu eti (mukuba)
Masuku pamutu eti (mukuba)
Mukumafuna katundu wanthu anzanukaaa
Mwayamba uhuleti (akazi waa)
Mwayamba uhuleti (mamaniwaa)
Mwayamba uhuleti (saankaziwa)
Nditalikileni social distance
Mix up