Ma File Lyrics
- Genre:Reggae
- Year of Release:2024
Lyrics
Ukakamba za ndalama sindichoka
Hustle timamenya sitimango talker
Khomo la opportunities takhala tiku knocka
Ukachedwa kutsegula upeza chitatchoka
Yachina we fulla goals ngati soccer
Ukamva waka sikuti kuli flocka
Osakamba sandalama ine ndima blocker
Ngati siiwe customer ndekuti ndiwe stalker
Ziwindi ngati Butchery
Sititrapa mockery
Ukadissa Mortuary
Mi hands fulla torturely
Sitipanga sorcery
Skill no lottery
Hustle ngati grocery
Undimvetse properly
When we rolling in the streets
Sitipanga Quit
Kuti tidye bread tilime kaye wheat
You know how we dweet
Sley wapinda beat
Mad rhymes I spit
Head hot like spliff
Ndimathamangitsa
Kuthamangitsa zima file
Mpake ndinasowa fi a while
Ndimathamangitsa
Ngati pali file
Number yanga utha kupanga dial
Zima file iwe zodzadza folder
Stock isanatheletu ndima crosser border
I am taking orders iwe uku chaser Rhoda
Utipeza kunja ndife asagoda
Ndimathamangitsa
Kuthamangitsa zima file
Mpake ndinasowa fi a while
Ndimathamangitsa
Ngati pali file
Number yanga utha kupanga dial
Imva ndikunenazi
Ine mfana focus
I am also known as
Mfana wa taking orders
We pop a couple sodas
Ndili konko as long as
Kuli zindalama zo tipange
Wul on
Everyday me working harder
Fi de pips weh call me Father
Mi dogs whey they angry the cross border
The hustle never stops olo kutada
Nafenso timafuna kuvala gucci olo prada
Mu street fufuza palibe satidziwa
Ife ndima savage azichimwene a Tiwa
Ukama dissa dziwa kwanu kukhala siwa
Anzanu analipo ndi awa anati zii wa
Matama ako sunga koma cash yanga vunga
Ticket nde takunga pa dheni tidya mpunga
Kimanso tikazisaka zina tima spender
Sitimadya zonse zina timasunga
Ndimathamangitsa
Kuthamangitsa zima file
Mpake ndinasowa fi a while
Ndimathamangitsa
Ngati pali file
Number yanga utha kupanga dial
Zima file iwe zodzadza folder
Stock isanatheletu ndima crosser border
I am taking orders iwe uku chaser Rhoda
Utipeza kunja ndife asagoda
Ndimathamangitsa
Kuthamangitsa zima file
Mpake ndinasowa fi a while
Ndimathamangitsa
Ngati pali file
Number yanga utha kupanga dial