Ndilipo Lyrics
- Genre:Reggae
- Year of Release:2024
Lyrics
Yachina
Inuyo mutentha bwanji ineyo ndilipo
Akazi akufuna abwele komwe tiliko
Zomwe amakonda zija kuno ziliko
Ife timayenda ndi dziko
Dancehall mu runner bwanji ineyo Ndilipo
Akazi akufuna abwele komwe tiliko
Zomwe amakonda zija kuno ziliko
Ife timayenda ndi dziko
Sixteen years in the game ndukusangalatsani
Ambiri anatha anangotsala makani
Anaka diss be? ma guy zachani
Samapenga nyimbo amapoka nkhani
Munkamenya bho koma vuto ndiloti
Iyi ndi yanga ploti
Ine ndi shatta poti
Ukhoza kufunsa Fada Moti
Ndima bragga poti Nadia ndi Nzanga poti
Player muna Bukayo kuno wau Saka poti
Ndimalowa zomwe ndafuna
Mufila musakufuna
Ma beat nde ndimangodya ngati lunch
Tricky ima kaye ndingomaliza kutafuna
Inuyo mutentha bwanji ineyo ndilipo
Akazi akufuna abwele komwe tiliko
Zomwe amakonda zija kuno ziliko
Ife timayenda ndi dziko
Dancehall mu runner bwanji ineyo Ndilipo
Akazi akufuna abwele komwe tiliko
Zomwe amakonda zija kuno ziliko
Ife timayenda ndi dziko
Malinga anatha mbali zakutiko?
Yaachina osa beba chaka chiticho
Lemme school these kids ine ndi teacher
Osamvayo ma pama ndine Adija
Mmmm ndimabwera ndi chi tool kit
Uka dissa zit blue tick
Gun Buss yeah futi
Badman man a shootie shootie
Ine sound ndima chapa
Style ili sharpa
Dancehall kunditsamila ngati logo ya Kappa
Mkazi wandipanga text what's for Supper?
Lero usaphike tidyela ma Rapper
Khala apa undimvetse proper
Kumasiyanitsa ma punch ndizi kwapa
Mento kuilowa ngati opposite ya upper
Drug sinditrapa koma cash
Inuyo mutentha bwanji ineyo ndilipo
Akazi akufuna abwele komwe tiliko
Zomwe amakonda zija kuno ziliko
Ife timayenda ndi dziko
Dancehall mu runner bwanji ineyo Ndilipo
Akazi akufuna abwele komwe tiliko
Zomwe amakonda zija kuno ziliko
Ife timayenda ndi dziko