Angola ft. Dr. Benedicto Wokomaatani Malunga Lyrics
- Genre:Others
- Year of Release:2023
Lyrics
Ndiwe mkazi okongola
Ndiwe mkazi okongola
Ndiwe mkazi okongola
Kuli konse ndikulondola
Kaya ndi Dollar ndikakongola
Kwanu Mumatchaja zingati lobola?
Ndiwe mkazi okongola
Kuli konse ndikulondola
Kaya ndi dollar ndikakongola
Ndidzakutengela ku angola
Ndidzakutengela ku Nyanja Ligineti
Ah huh
Zoti ine ndimakukonda si sikileti
Ah huh
Umandiwaza ukavala Mini skirt
Ah huh
Zoti ine ndimakukonda si sikileti
Ah huh
Kwawo anamulanga asanalakwe
ndi wa nyatwa wa khalidwe lake
My friends amangoti I am lucky
Mkazi wako yi alibe mzake?
Ndakaona pa corner ndakaitana
Talking stage tungo vybana
Ndikadona kakugulu sizo hidana
Wife her true I wanna
Olo Beyonce atati mu sizane
On you I will put my money
You too sweet yeah you my honey
Kundisiya me I will Hibernate
Ndiwe mkazi okongola
Kuli konse ndikulondola
Kaya ndi dollar ndikakongola
Ndidzakutengela ku angola
Ndidzakutengela ku Nyanja Ligineti
Ah huh
Zoti ine ndimakukonda si sikileti
Ah huh
Umandiwaza ukavala Mini skirt
Ah huh
Zoti ine ndimakukonda si sikileti
Ah huh
Ndidzakutengela ku nyanja Ligineti
Titsagane ku Mangochi Ligineti n'kakuonetse kukoma kwa Nyanja
Nkakuululire zogona mu mtima wanga
Zomwe ndimakhumba ntakuchitila iwe
Chakudya cha Maso Anga