La Vida Loca Lyrics
- Genre:Reggae
- Year of Release:2021
Lyrics
La Vida Loca - Malinga
...
yah min
been working all my days ndipumeko for minutes mmmmh
lero ndizipepese
hardwork don't need it ooh
been working all my days ndipumeko for minutes
lero ndizipepese
lero nde lero nde tiuchapatu
kuchita kuuyamba kuchita kuwuyamba mamawa chamma 2
backyard ndungotchila ndianzangatu
nagt shower tiusambatu
lero nde lero nde tiuchapatu
kuchita kuuyamba mamawa chamma 2
phone ring ghettoh call me from frnd Dem say, bwera ndi mikunda 2
chorus
lafika lokha Friday
so me tell you that life is good, La Vida Loca
ngat mukupita kunyumba, mupita nokha
so me tell you that life is good, La vida loca huh huh
lero tizipepese
koma lero tizi mwere, muuzeni wangongole akagwere, ma frienzo abwere
amwene mavuto sazatha
koma lero tizimwere,
muuzen landlord akagwere, ma frienzo abwere vunga ina ase
bills on me mwere
muuzen wangongole akagwere, ma frienzo abwere
muuzen landlord akagwere, ma frienzo abwere,
tizipepese
tiipemerere