Chete ft. Zeze Kingston Lyrics
- Genre:Reggae
- Year of Release:2024
Lyrics
Siine Dollar sindingakondweletse nonse
Olo mutinyoze
Zilibe ntchito iPhone or mose
Mpweya timapuma tonse
Chitsotso cha mu diso mwako usanachotse
Cha mu diso langa usachiloze
Mukavala inu mumaitcha Swagg
Tikavala ife mmmh ma Lacoste
Kodi uyu dollar amazitenga pati?
Zaku Nyumba kwanga Zakukhudza pati?
Tisafunsane kuti uyu walowa bwanji
Ma guy bola tonse tili mkati
Aliyense pa Malo pake chete
Pa malo pake chete
Aliyense pa Malo pake chete
Pa malo pake chete
Muzipanga zomwe zimakusangalatsani
Chete
Afuna tigwe cholinga atiseke
Koma Jah Jah akutikweza ngati Jeke
Criticism ndi nsanje
Sizimasiyana kweni kweni
Samala ndi amene udya naye
Pa table pamakhala fork ndi mpeni
Amakuphweketsa ngati akuseka
Pansi pa mtima akunena zeni zeni
Uja munkamuti Nzanu weni weni
Ali kuti pano mutayamba geni
wandipeza online, zone yaine, phone yaine
Ring ring ring tone yaine
Amanama amandikonda ine
Koma pansi pa mtima akundizonda ine
Aliyense pa Malo pake chete
Pa malo pake chete
Aliyense pa Malo pake chete
Pa malo pake chete
Muzipanga zomwe zimakusangalatsani
Chete
Afuna tigwe cholinga atiseke
Koma Jah Jah akutikweza ngati Jeke
Paja zikakanika ndiye kuchulukitsa nkhani
Ngati zili zophweka bwanji zikukanikani
Monse mwayambila ku zungulira ngati fan
Ife timangopanga olo opanda Pulani
Ndiye ndipange ichi basi ndakupatsa nkhani
Kuchita kukokelera chidani
Mpakana kundipekela nkhani
Cholinga ndikayankha ati ndiine wamakani
Ali ndi mwana amugwilitse
Pa malo pa ndivinitse
Ali ndi mwana amugwilitse
Pa malo pa ndivinitse
Aliyense pa Malo pake chete
Pa malo pake chete
Aliyense pa Malo pake chete
Pa malo pake chete
Muzipanga zomwe zimakusangalatsani
Chete
Afuna tigwe cholinga atiseke
Koma Jah Jah akutikweza ngati Jeke