ALIPOMPO Lyrics
- Genre:Reggae
- Year of Release:2023
Lyrics
Rising to ditop Benghinifiscent family
Benghie man ah complex, rising gangster
Benghazzie, spit out lyric hotter dan ah bullet fram dem gunzie
Ndife achoncho, ndimmene tilili
Nkazi, wafila gangster
Wapenga ndi chikondi chomwe ine ndimamupasa
Tonani mwanakazi, angofila
Paliponse pomwe ndili naye ali pompo
Nkazi, wafila gangster
Wapenga ndi chikondi chomwe ine ndimamupasa
Tonani mwanakazi, angofila
Paliponse pomwe ndili naye ali pompo
Nkhani zachikondi chiBenghazzie ndichimakina
Sizongopakana Zanga sizongokhalila kukangana
Ndine sativa pretty galis wapenganane
Komedwanane, nkazi wagomanane
Ndipo mu dancehall ndakwela lader
Ndine Benghazzie dada wa ma dada
Ine ndi kinka, glaber, ndine jada
Kung fu dancehall ndine master
Kapena ukufuna ndikusinthile styli kodi
Chapatali kumango bwekera, lilira, kopela
Ati Benghazzie dancehall ikumagona dojo kodi
Ine ndi gangsta diss sinzasiya
Nkazi, wafila gangster
Wapenga ndi chikondi chomwe ine ndimamupasa
Tonani mwanakazi, angofila
Paliponse pomwe ndili naye ali pompo
Nkazi, wafila gangster
Wapenga ndi chikondi chomwe ine ndimamupasa
Tonani mwanakazi, angofila
Paliponse pomwe ndili naye ali pompo
Mi nuh get ah single pretty gyal, mi get ah bungle
Get dem out ah road, man ah get dem ina jungle
Ah nuh try, try, get di gyal dem ina one go
Gyal ah want mi, see dem watch mi though di window
Akapasule, mukuchepa
Kubwela 4,4, ine kukupa
Chi Benghazzie sichitekese
Ine kutuluki inu ntima kugunda
Avakasheni, avakasheni
Azungulile ground mpaka ka 10
Asajaile nginiyi ndiya pa den
Lobadwanalo luso langa, sinnapite kuskulu
Nkazi, wafila gangster
Wapenga ndi chikondi chomwe ine ndimamupasa
Tonani mwanakazi, angofila
Paliponse pomwe ndili naye ali pompo
Nkazi, wafila gangster
Wapenga ndi chikondi chomwe ine ndimamupasa
Tonani mwanakazi, angofila
Paliponse pomwe ndili naye ali pompo
Nzaki, watichani?
Wati ufuna nzikupanga chani
Wabwa mmene ikubwerera, mvekera, bebera Dancehall yi
Ngati tizokudya tabwino tabwino, matchingitchani