KWA INE Lyrics
- Genre:Others
- Year of Release:2024
Lyrics
Benghazzie,
Chi Benghazzie
Bad gyal pretty face, you alone ah my type
Come close hold mi tight you ah gi mi good vibe
I will alwys do you right if you stay by my side
My love is your right, your body is my ride
Call you, text you, when i miss you
Please say yes, gyal i wanna to wife you
Am only special coz am always gonna have you
Worl full ah gyal i will always choose you
All eyes on you when you miss behave
Mash up mi mind, body full ah curve
Your love for me is more than i deserve
Am lost in you i can not be saved
Kwaine, ndiwe namba wani
Palibe wangati iwe
Kwa ineyo ndiwe namba wani
sinzampeza oposa iweyo
Ngati iweyo, ngati iweyo
Ngati'weee, weee, weeeyo
Fire, fire gyal your body fire
Kay, kaya, nkhaku dokesye ku kaya
Taya, taya ine sindidzakutaya
Shuga, honey, mutuwane wa taya
Wasala onsewa nkazi wasankha chiBenghazzie
Man ah full ah love like ah trailor load ah gunzie
Kundipengesa dzina lako lingokhala nazi
Tchuzi kaye, fufuta ndanenazi
Nkazi okongola khalidwe ngakhale pa chithunzi
Chiphadzuwa, moyo upume, ntima wapeza nthuzi
Chikondi chokwana ndileke kumangila nkhuzi
Ndizeni zeni sizongokuvula ngati juzi
Kwaine, ndiwe namba wani
Palibe wangati iwe
Kwa ineyo ndiwe namba wani
sinzampeza oposa iweyo
Kodi nkazi,ntima ugunde bwanji
Kuti iweyo udziwe nthiti ndi iweyo
Iwe nkazi, tanditaye paliponse
Koma sangakonde kuposa ineyo
Namwali,mpaka ku? mpakamndende
Paliponse, ndzakutsata kumalembe
Tchimo lanji tanena tichimwisane
Thawisane, kukonda kukonda, tipikisane
ukukayika pati
Chani chingakome kuposa mmene ndikukondelamu
Tupange makwati
Chikondi chokhalisa sizangatiza sugar bubble gum
Kwaine, ndiwe namba wani
Palibe wangati iwe
Kwa ineyo ndiwe namba wani
sinzampeza oposa iweyo
Kwaine, ndiwe namba wani
Palibe wangati iwe
Kwa ineyo ndiwe namba wani
sinzampeza oposa iweyo
Ngati iweyo, ngati iweyo
Ngati'weee, weee, weeeyo