DAMEJA Lyrics
- Genre:Hip Hop & Rap
- Year of Release:2024
Lyrics
Eh, aye, aye, khala bwanji
Bebie yoti timatchila bwinobwino
Namba yake ndinatenga bwinobwino
Timalinkana, timatextananso
Ndikudabwa pano bebie igwanda
Ah, akudameja ndindani
Eeh?, kudameja ndindani?
Esh, akudameja ndindani?
Aku-thila dameji ndindani?
Boys, kodi zikukhala bwanj
Nkazi ololalola andikanilanji
Dzulo anandikhola, lero wandi blokelanji
Wakwiyilanji, Kwawo wandileselanji
Pali winawake yemwe akusokone-za
Nkadzapeza nzamuponda, kumugudumu
Ngatimulipo kagulu pitani mukauzane
Nsazakuone, ghetto tisazakumane
Bebie yayamba kunyada
Akandituluka ndzatibula kape yemwe adzagwileyo
Koma ngati ali ex
Nane ndidzijama yake, ndi zoba wakeyo
Bebie yoti timatchila bwinobwino
Namba yake ndinatenga bwinobwino
Timalinkana, timatextananso
Ndikudabwa pano bebie igwanda
Ah, akudameja ndindani
Eeh?, kudameja ndindani?
Esh, akudameja ndindani?
Aku-thila dameji ndindani?
Bebie yoti timatchila bwinobwino
Namba yake ndinatenga bwinobwino
Timalinkana, timatextananso
Ndikudabwa pano bebie igwanda
Ah, akudameja ndindani
Eeh?, kudameja ndindani?
Esh, akudameja ndindani?
Aku-thila dameji ndindani?
Koma nkazi nde wanyadatu
Sindikuwonanso chifukwa choti ndikukakamile
Sizinzli zoti mpaka ndzakufelatu
Mtma wanga sunawine, bomgo sunasokoneze kagwele
Zuti bwanji mfana okhomele
Nkazi uja anabwela ndiyochondele
Kutumiza tazinkake kundinyengere
Ati tiyese kachikena ndiwone mmene andikondere
Mukufuna mzindipatsa preasure
Mukamandi phwekesa, pena zimandisekesa
Mwakanika kugwetsa,pano simukumetsa
Ndine Shuga boy nkazi sakufuna kubetsa
Bebie yoti timatchila bwinobwino
Namba yake ndinatenga bwinobwino
Timalinkana, timatextananso
Ndikudabwa pano bebie igwanda
Ah, akudameja ndindani
Eeh?, kudameja ndindani?
Esh, akudameja ndindani?
Aku-thila dameji ndindani?
Bebie yoti timatchila bwinobwino
Namba yake ndinatenga bwinobwino
Timalinkana, timatextananso
Ndikudabwa pano bebie igwanda
Ah, akudameja ndindani
Eeh?, kudameja ndindani?
Esh, akudameja ndindani?
Aku-thila dameji ndindani?