ADADI ACHOKAPO Lyrics
- Genre:Hip Hop & Rap
- Year of Release:2024
Lyrics
Eeeh, Benghazzie
Mutisokose fukwa adadi anu achokapo?
Mutibowe paja adadanu achokapo
Pushenjale, paden adadi achokapo
Paja amasiya change akamachokapo
Weekendiyi ndemwatasatu, paja adadi kulibe
Guza njale ya payard, nfana kudzimva uGide
Mpaka spray wa adadi, mwaganiza zoti mumube
Easy, sitidzanena, sizoti mpaka mutide
Nfana kuthoka chomene, njibwa nfana kuphwekesa ngini
Bolling mpila wa paper, zoba lero opopa kulibe
Kachizungu kongo gwera, umangobela sutsata ngini
Tisilile za adadizo? nthawi imeneyo tilibe
Mutisokose fukwa adadi anu achokapo?
Mutibowe paja adadanu achokapo
Pushenjale, paden adadi achokapo
Paja amasiya change akamachokapo
Mutisokose fukwa adadi anu achokapo?
Mutibowe paja adadanu achokapo
Pushenjale, paden adadi achokapo
Paja amasiya change akamachokapo
Dikila adadi abwere, mafana olubwa aleke kunjanja
Dikila adadi abwere, tione ngati mutafupenso nyau
Dadi kubwera, kubawa kwa dairy kuja muyambe kujomba
Dadi kubwera, mafana kuthoka mopusa adadi kunyapula
We dont hung around with little kids, opempha dola adadi akamachoka
We dont chill, we dont click, ndimafana ongojaka mdala akachoka
Mfana usandipatse busy, you got pckets full of holes
I got more money than banks in the villages, i'll be smelling like a volt
Mutisokose fukwa adadi anu achokapo?
Mutibowe paja adadanu achokapo
Pushenjale, paden adadi achokapo
Paja amasiya change akamachokapo
Mutisokose fukwa adadi anu achokapo?
Mutibowe paja adadanu achokapo
Pushenjale, paden adadi achokapo
Paja amasiya change akamachokapo