VINIPHONYE Lyrics
- Genre:Others
- Year of Release:2023
Lyrics
Ivi vama love, vama sweetheart
Ulendo uno okha vindiphonye
Vomapangana noney,darling, chocoalate
Mtima wanga ukukana
Ivi vama love, ma relationship
Ulendo uno okha viniphonye
Voti nikhale boyfriend, kukonda girlfriend
Mtima sukugwirizana navo
Ati how are you baby-boo
Ndakusowa, how do you do?
See you later, i love you too
My heart and soul belongs to you
Ukukamba vosevi uli ndi wina
Baby-boo naye ali mmanja mwina
Ndi chikondi cha bwanji? sindikumvetsa ndine mwina
Relationships, kuwawisa mtima
Ivi vama love, vama sweetheart
Ulendo uno okha vindiphonye
Vomapangana noney,darling, chocoalate
Mtima wanga ukukana
Ivi vama love, ma relationship
Ulendo uno okha viniphonye
Voti nikhale boyfriend, kukonda girlfriend
Mtima sukugwirizana navo
Va malavu mpaka ayenda mu ng'anga
Funa wachikondi ayenda mu ng'anga
Asazalekane naye ayenda mu ng'anga
Banja, ng'anga, mwana, ng'anga
Koma pena vimatha kukhala veniveni
Love ndikubeba, kuzafika penipeni
Kummawuzana ndzakufela vili veniveni
Kusowana kulira, kukondanadi kwenikweni
Kenako akaduka, alowelerepo
Tumaroumers tikuvizitepo
Kuyamba kusaka chingwe, kufuna kudula mphepo
Bola kukhala single, life ili simple
Ivi vama love, vama sweetheart
Ulendo uno okha vindiphonye
Vomapangana noney,darling, chocoalate
Mtima wanga ukukana
Ivi vama love, ma relationship
Ulendo uno okha viniphonye
Voti nikhale boyfriend, kukonda girlfriend
Mtima sukugwirizana navo
Ivi vama love, vama sweetheart
Ulendo uno okha vindiphonye
Vomapangana noney,darling, chocoalate
Mtima wanga ukukana
Ivi vama love, ma relationship
Ulendo uno okha viniphonye
Voti nikhale boyfriend, kukonda girlfriend
Mtima sukugwirizana navo
Kukhala single salesana
Ngati ndikukondwa ndilekeni
Khala single salesana
Ngati ndikukondwa ndisiyeni
Kukhala single salesana
Ngati ndikukondwa ndilekeni
Khala single salesana
Ngati ndikukondwa ndisiye
Ivi vama love, ah heee
Ivi vama love, ah hooo
Ivi vama love, vama sweetheart
Ulendo uno okha vindiphonye
Vomapangana noney,darling, chocoalate
Mtima wanga ukukana
Ivi vama love, ma relationship
Ulendo uno okha viniphonye
Voti nikhale boyfriend, kukonda girlfriend
Mtima sukugwirizana navo
Ivi vama love, vama sweetheart
Ulendo uno okha vindiphonye
Vomapangana noney,darling, chocoalate
Mtima wanga ukukana
Ivi vama love, ma relationship
Ulendo uno okha viniphonye
Voti nikhale boyfriend, kukonda girlfriend
Mtima sukugwirizana navo