NDIKUYENDERE Lyrics
- Genre:Others
- Year of Release:2023
Lyrics
Mami nkakuwonani
Usikuwonse n'makulotani
Zenizeni, ndakupangilani maplan
Watimbu? panga zoti timvane
High grade gyal, ndikufuna ndikubande
Badman love, mwela nsuzi ngati dende
I, like you mpaka handede
Wanna keep you warm ngati blangete
Udzangodusa paden utavala ka mini
Kuti me and my boys tikuKambe
Titamvana ziwiri, ndikuthekesa ngini
Twee pano, palibe angadzalande
Nthawi zonse ndikakuwona, ngini yanga umayibanikisa
Maka maka ukayandikila, zimafilu umadzipatsa moto
Ndimafuna ndikuyendere
Ndimafuna ndikuyendere
Nthawi zonse ndikakuwona, ngini yanga umayibanikisa
Maka maka ukayandikila, zimafilu umadzipatsa moto
Ndimafuna ndikuyendere
Ndimafuna ndikuyendere
Uli boh, uli good, uli bwino
Hot beverage ndiwe capachino
Guy got love, funa udziwe lerolino
Seriously, tikwatire chaka chino
Pretty mama panga zoti ndikuyendere
Dream gyal got me day dreaming
Getting wild ngati moto wamu thengere
Stick round, I'll be cool for the chilling
Mmmmh waniko wanipweteka
Mtima, nthiti zonse ndikupereka
See, I got free time and you got free ime
Ndikulondore, ndikuyendere
Nthawi zonse ndikakuwona, ngini yanga umayibanikisa
Maka maka ukayandikila, zimafilu umadzipatsa moto
Ndimafuna ndikuyendere
Ndimafuna ndikuyendere
Nthawi zonse ndikakuwona, ngini yanga umayibanikisa
Maka maka ukayandikila, zimafilu umadzipatsa moto
Ndimafuna ndikuyendere
Ndimafuna ndikuyendere
So, you like me too, nde titanino?
Nditha kukupengetsa ndichikondi, tenge bwino
Panopano gokonko kwanu konko
Day well spent, mpaka kufuna kugona konko
Bankilikicho, muntima mwakono
Paliponsepo, khwasyepo, nozyepo
Ndifatsepo zozuna lawepo
Ngati pali vuto tanena tiwonepo
Dziwa, zachikondi ndine makina, mtchini
Kukupatsa chikondi mpaka uledzere, gin
High fever, ndine wako panado, khini
Dzimafilu kuponya mabandulo