Wonna Be Lyrics
- Genre:Hip Hop & Rap
- Year of Release:2024
Lyrics
Ma guy'wa ati ndi ma role models
Nkhani kugugudiza patron bottles
Their ways are misleading but so subtle
Live fast die young yolo right wrong motto
Akumakutila umve ndizokometsa
Kumakongoletsa mfundo zosokoneza
Akamabwera ndi bodza kunong'oneza
Ife tikatsutsa ati tikukokomeza
Ma celeb wa timawakondetsetsa
Don't let the fame blind you though kumaonetsetsa
Ali ndi zinthu zawo zokondweretsa
Koma mukaonetsetsa zina n'zosocheletsa
Osamangotengela kumachenjela
Mukakana moyesera muzatsatira mbwelera
Enanso amazithemba opemphera
Koma chonde osasekelera mfundo zopepela
I desire many things
But nothing can compare to the king of kings
It don't matter what this world here tell us
Unashamed and we zelous hommie I just wonna be like
Jesus Jesus Jesus Jesus
Sitisilira dziko ndimafuna kukhala ngati
Yesu yesu yesu yesu
Yesu yesu yesu yesu
Udolo ku dziko ndi moyo wa chisawawa
Kumazimva udolo koma uli cowa ward
Gist yomwe amayitenga yakawawa
Ndi moyo wa chisembwere komanso kumwa bawawa
Chilungamonso amachithawawa
They know the savior but deny his power wow
Zoyaluka ndisaname zimawawawa
Kuona role model koma ma scandal ndi phwamwamwa
Zili zonse sitingamangotsanzira
Olo tizinenedwa otsalira
Tinapeza shasha wathu omutsatira
Mawu oyera ali ndi zitsanzo zokwanira
We on fire for yahwe ngati mafuwa
Ndipo celeb mwa ine sindingampatse guwa
Follow the son ngati afana otsata dzuwa
Anyoze yea sure timatsata Yeshua
I desire many things
But nothing can compare to the king of kings
It don't matter what this world here tell us
Unashamed and we zelous hommie I just wonna be like
Jesus Jesus Jesus Jesus
Sitisilira dziko ndimafuna kukhala ngati
Yesu yesu yesu yesu
Yesu yesu yesu yesu
I desire many things
But nothing can compare to the king of kings
It don't matter what this world here tell us
Unashamed and we zelous hommie I just wonna be like
Jesus Jesus Jesus Jesus
Sitisilira dziko ndimafuna kukhala ngati
Yesu yesu yesu yesu
Yesu yesu yesu yesu
I just wonna be like
Jesus Jesus Jesus Jesus
Sitisilira dziko ndimafuna kukhala ngati
Yesu yesu yesu yesu
Yesu yesu yesu yesu
Ey you know what we on bro we all zelous
Ain't trippin for no idol mayne my God jelous
They got bunch of lies that they tryna sell us
But we ain't never buying what they tryna tell us