
Mbwee Lyrics
- Genre:Hip Hop & Rap
- Year of Release:2019
Lyrics
Yea yea
Yea yea
Oh yea
Fanzi ikufunsa fanzi ikudabwa ati ndikuwala mwachilendo
Kubeba kokhako chimfana chikuwala kuchoka kumutu mpakana kumwendo
Yea,they look at the swagger, and come up with bunch of conclusions
They don't know Jesus the Christ is the one that I credit for all my solutions
Aise aise aise aise ndachoka patali
Ndipo sizikanatheka kuti ndifike lero popanda yesuyo pambali
Nthawi zina sizinali bho bho
Koma dolo wa ma doloyo anali pompo
Kundigwilitsitsa kuti ndisakomedwe ndi zotsala poti zobalalitsanso zinali thotho
Mukamandiona, ndikulimba chonchi, nkhani si udolo koma yahwe
Ndipo nthawi zina, ndimabalalika, koma mbuyeyo sanandithawe
Kaya ndi ziphinjo takumana nazo kufika tsiku lalero siphada
Ndipo n'nakakhala, ndimayenda ndekha, bwenzi pano nditagwa chagada
Yea,zimayesero pali ponse nde ndi mbwe mbwee mbwee
Zokomedwetsa nzosayamba nde ndi mbwe mbwe mbwee
Kubalalika n'kosayamba, yea ndi mbwe mbwe mbwee
Koma zisomo za chautayo ndi mbwe mbwe mbwee
I got issues, I got issues osayamba
Zimavuto ndili nazo osakamba
Koma chikondi cha chauta osayamba
Koma zisomo za chauta osakamba
Zili mbwee mbwee mbwee, zili mbwee
Zisomo za yehova nzosayamba zili mbwee
Zili mbwee mbwee mbwee, zili mbwee
Zisomo za yehova nzosayamba kuti mbwee
Nde ndikamati ndine khristu, amaona ngati n'nazitolera
Yah Mukamandiona chonchi ndi chisomo cha yesu khristu chimene anandionetsera
Oh yea oh yea takumana nazo zikhomo
Yea,mukamandiona ndikulimba siumakhala ushasha koma mphamvu ya zisomo
Zimachimo mbwe mbwe mbwe
Zimavuto zi ma issue zili mbwe mbwe mbwe
Yea,Koma anandikoka ndikuchotsa mumdima pano ndinayera mbe mbe mbe
Ya ya ya ya siine dolo nje nje nje
Ndine kapolo wa chabe chabe ndipo anakandisintha cholinga chake kuti tifanane nde nde nde
Was heading for doom, ngati ndine mphemvu
Ndili ndi yahwe, pano ndili safe
Mwini wake game, ndimayenda ndi ref
Ndili ndi shasha, sindipanga befu
Udolo pa mbali, sizimatengera kuchenjera
Nd'choka patali, yankho langa ndi yahwe zikamandiyendera
Akanafuna, akananditaya
Ndi chifundo chabe mbuyeyo samandiswaya
Mukamandiona ndili chonchi musamapusitsidwe amandisunga ndi messiah
I got issues, I got issues osayamba
Zimavuto ndili nazo osakamba
Koma chikondi cha chauta osayamba
Koma zisomo za chauta osakamba
Zili mbwee mbwee mbwee, zili mbwee
Zisomo za yehova nzosayamba kuti mbwee
Zili mbwee mbwee mbwee, zili mbwee
Zisomo za yehova nzosayamba zili mbwee
Zili mbwee mbwee mbwee, zili mbwee
Zisomo za yehova nzosayamba kuti mbwee
Zili mbwee mbwee mbwee, zili mbwee
Zisomo za yehova nzosayamba kuti mbwee
Kuti mbwee
Kuti mbwee
Kuti mbwee
Kuti mbwee