Palibe Kubetsa Lyrics
- Genre:Hip Hop & Rap
- Year of Release:2024
Lyrics
Amandinena ati n'nakali wamn'gono
Ndisabetse chinyamata ati ndinjoye pang'ono
Ati za mulunguzi tizazipeza
Ati chi khristu uli mfana ndi kubetsa
Palibe ndimasowa palibe kubetsa
Ena amangotalka sangathe kumvetsa
Am gonna make it yesuali pa mpando
He's always got the answer ndilibe madando
N'katengeka nzoipa
Zinkaoneka bho zili zotchipa
My God major let me go deeper
Goli anamasula like a fasting goalkeeper
Yea ndakhala pa dzikoli
Oipa wandiimba ngati mingoli
Wuuh n'nazitaya za dzikoli
Anandisaver ngati keeper kuchotsa chigoli
Palibe kubetsa zonse ndimafunazo ndinazipeza
Palibe kubetsa zonse ndimafunazo ndinazipeza heeee

Ndikaona m'mbuyo lerolo sinnakafika
Siushasha ndi chisomo zinazi ndinazitsika
Ine ndekha nde sindimanamizika
Nde nginiyi sindimapangila kukakamizika
Tinapeza peace madalitso bonus
Koma ati timataya nthawi ndi zobornaz
Ife timatsata zoonazi
So woke sitimapanga zogonazi
Amazakutenga zobazi
Maka ukakana zomwe fanz imakondazi
But we got a different test
Nde sitimatengeka ndizooneka zononazi
Tilibe mantha kukakwera pamalata
Uthenga ndi kupantha about the living water
The hate will never matter kwa omwe sazitsata
Sangamvetsetse za bata tinapata pomutsata