Dancehall ft. Crispy Malawi & Lil AL Lyrics
- Genre:Hip Hop & Rap
- Year of Release:2023
Lyrics
Ngini yathu timayendetsa mwa manual
Mmmmhmmm
Tapanga zoti, ti runny dancehall
Mmmmhmmm
Tapanga zoti, ti runny dancehall
Mmmmhmmm
Tapanga zoti, ti runny dancehall
Yuh
Ngini yathu timayendetsa mwa manual
Mmmmhmmm
Tapanga zoti, ti runny dancehall
Mmmmhmmm
Tapanga zoti, ti runny dancehall
Mmmmhmmm
Tapanga zoti, ti runny dancehall
Ndilibe nazo olo atati panga cancel
Koma zau bate ndima dana nazo
Nayamba kuyimba chonchi zisali mu fasho
Nde, sitinga yambe kuyika amapiano eh
Tabwela pano ase ndikuwuze nthano eh
Uka panga mwano tikuchosa mano
Ndine wa kano ndati ndine wa kano
Ndinayambitsa toxic masculinity yeah
Tachosa tinyimbo tatoko tafaka thako
Uhuh
Mafana ambiri sakusata dancehall
Uku sikuimba ndiku pusher hustle
Ndufuna benz sindikufuna passo
Aaaah
Amkati Tungosuta ZaZa
Eya Sindingakane Man Ndimkangosuta Zaza
You know How it Feels
Uli ndi Plan Koma ulibe Ndalama
Pano ndi In & Out The City Ma Babe akudanda
Ati Akufuna Za dama Uhuh
ine ndili Busy Ku chaser Zi Ndalama uhuh
Ku Flipper Dancehall kumenya Zima Backsummer
kufika Ndima Vybz Azim Adidja Palmer
Famous Tenga Gun ti shooty ma Informa
Spe For presidente Mario bros Boma
Amatifila Ma Gee Achina Vide ndi Madonna
Ndili ndi Gang Tiku Trappa Chapa Corner wamva
Ngini yathu timayendetsa mwa manual
Mmmmhmmm
Tapanga zoti, ti runny dancehall
Mmmmhmmm
Tapanga zoti, ti runny dancehall
Mmmmhmmm
Tapanga zoti, ti runny dancehall
Yuh
Ngini yathu timayendetsa mwa manual
Mmmmhmmm
Tapanga zoti, ti runny dancehall
Mmmmhmmm
Tapanga zoti, ti runny dancehall
Mmmmhmmm
Tapanga zoti, ti runny dancehall
Ngini yathu timayendetsa mwa smart
Sima stunt
Titha kupanga rant
Ngati tat
Ma skin zikufwamba ndati
Kuzifeela mati mati
Nkati nkati
Ukubwera ndikati
U superstar ndi uwuwu
Usayese zovala
Oho
Uzingomva ululu, ngati ukwati wanga
Oho
Timabwera gulu, ndikumeta mpala nkhanga
Ku Runner road Koma Siti pala
When you see we, tu chitawira
Moto man
Beya, Koma kicks yanga shotokan
Osakoka nkhani
Tangokonza plan
Tinangodya one
Mulipa ngodya man
Ngini yathu timayendetsa mwa manual
Mmmmhmmm
Tapanga zoti, ti runny dancehall
Mmmmhmmm
Tapanga zoti, ti runny dancehall
Mmmmhmmm
Tapanga zoti, ti runny dancehall
Yuh
Ngini yathu timayendetsa mwa manual
Mmmmhmmm
Tapanga zoti, ti runny dancehall
Mmmmhmmm
Tapanga zoti, ti runny dancehall
Mmmmhmmm
Tapanga zoti, ti runny dancehall