Krazie Knights ft. Jeff Nyimbo Lyrics
- Genre:Hip Hop & Rap
- Year of Release:2023
Lyrics
Mwachulutsa kubleyetsa
Mungogawa ma pillow
Ukasaka Mario Bros Ikulembani ntchito
Ngati sunamve verse yanga
Ndekuti ma kwacha ndi zero
I'm connected like the plug
Mboni yanga ndi Philo
Chilichonse covered Zofunda
Mukubleyetesa, zofunda
Mukubweretsa, zovunda
Mukubwereza, zokuda
Ndichi babe changa, chozuna
Drip ndi mbedza, zofuna
Sharp ndi razor, zokutwa
Ndasweka ngati ntedza
Abale samalani
Ngati good samaritan
Ndikungopha ma rapper
Ma beat asamale ndani
Kuli ma white flag ngati ndango surrender
King Katakwe Krazie KKK akama ngena
Dressed in all white
Ngati nagwera mu ufa
Kuphazi kuli Nike
Iwe sapato wagufa
Dzima banger zingobwera
Uzingosintha subwoofer
Ndili ma jam ndi butter
Ndikungosaka bufa
Ndadya Ka ganja kolusa
Ma goat tikukusa
Kugawa zinyimbo kapusa
Iwe Ukuchanta Tadutsa
Ma Bebi amandifila ndinanena kale
Kambayu ndufuna kuphaka nde sindigawe
Uyiwonelera ngati sukuyitolera
Amakhomelera ukayamba kuyiwonetsa
Mkazi Sali straight ku room kumukhotetsa
Wandipatsa Head
Wandipatsa
Wandipatsa
Ndipase beat yo ndilembe
Ma style ndi plenty
Kulinker ndi Pun, ndi Gwetse
Beamer yo tikwele
Boys yakoyo si ifeyo, Ifeyo ndi ifeyo
Size yako si ineyo, tikalinker zisamatelo
Usazipanikize ungokhala phee
Usazibalalitse uziyika mpeni
Usazayitole nthumba singakwane
Ndizovaya Abrazi sindingakhale