Balenciaga Lyrics
- Genre:Hip Hop & Rap
- Year of Release:2023
Lyrics
Ndiza uslave Sindidzavalaso chain
Malawian Drip, Katakwe Amen
Ndingo dropper ma tracks mubwere ndi ma train
I'm stoned I'm Abel & I Cain
This ain't no cap kumutu kuli dread
Ndavala too ghetto too Gattah, ndingo saka bread
Ndamuvula wig akupeleka head.
A…. ndinamaliza, Z
Connected I tether
Whatever is clever
Jacket ndi leather
Chifukwa cha weather
Chick nda Sosola feather
Pano ndingosaka Cheddar
Ndukuuza mi Breda
Mmene ndavalira ndimmene ndikumvera Mmene ndimayimbira ndimmene ukumvera
My profits go deeper uthakugwera
Ine Addi Di Teacher ukuyenera kugera
Umaganiza bwanji? Zaza burner? Paliponse ungokamba za hustle
Umavala zako koma umatchena
Ndadabwa nditakuona pa maso
Balance yanga
Siya Balenciaga
Balance Yanga
Siya Balenciaga
Balance Yang
Siya Balenciaga
Panga zako mfana
Gang sporty numbers zakuma Lotto
Glove punch Miguel wayika cotton
Chili chonse ndi chodula ntengo wa cotton
Colon ndi zaza, ndakumana ndi popo
Balance the jager
2 shots. Tizipita
New Balance wanga
Wa jaja wapona kitta Balenziaga
Sitivala zotchipa
Mb'ale si yanga
ndingodya modikiza
So if this is the perfect example, we can conclude that the whole thing is just normal
Wavala zovala zoti zitha kuku chapitsa
Wangomenya ma phyzo wasanduka cholapitsa Mario Brrr Gang sound kuphulitsa
Kutchena ndikugula zomwe Ife tikugulitsa
Ndavala Gucci ndukuuzani atsogo
Olo Versace nsalu ya apongozi
Underamour Ndili mkati mwa ubongo
Zabwino Avale, bale ndi alongo
Imma tell you like Wu told me
Umaganiza bwanji? Zaza burner? Paliponse ungokamba za hustle
Umavala zako koma umatchena
Ndadabwa nditakuona pa maso
Balance yanga
Siya Balenciaga
Balance Yanga
Siya Balenciaga
Balance Yang
Siya Balenciaga
Panga zako mfana osati zanga