ZaZa ft. Crispy Malawi Lyrics
- Genre:Hip Hop & Rap
- Year of Release:2023
Lyrics
ZaZa ft. Crispy Malawi - Krazie G
...
Izzy tili pa easy( checks, tipase ZaZa)
a wiz-a, a wizzy abwera
Zaza, Zaza
Tungosuta Zaza, zaza
Chimwemwe chango Zaza
Ndili ndima Shasha,
Ina ili mmanja, Ina ili mu bag, ndango shava
Tungosuta Zaza, Zaza
Zaza, Zaza
Chimwemwe chango Zaza
Ndili ndima Shasha
Ina ili mmanja Ina ili mu bag ndango shava
Ndimamvana ndi mmodzi, koma alipo awiri
Milomo yada biii, ngat ndayipaka kiwi
el dash Smoking ndi Kacha ngat kwa biwi
ATI Crispy uli Krazy, ndat ndimamvana ndi Fini
I've been smoking large, Chibwezi chatha mwachinsisi
She been stressing out, mpaka ku bhollera fees
You can't faze me out, the chosen can't be defeated
Kubwela kwanu ndi Gang, ukafina undi beefe
Ndakhalira kusuta Zaza since morning, ndifunika munches
Ndili ndima juice mu trap, mtengo wama Nanchesi
Ndili ku 21, Chilinde, osati Savage
Nli mma choice awiri, filla spear or kumwa tamek
kudusa Santa plaza, kuvaya 18 kuyang'ana, (Zaza)
kuyituluka ghetto, yangozaza ndima (Zaza)
Ine ndimaimba, ma babe amango flasha
Still in love with Mary-Jane Mumuwuzeko Natasha, kut ndungofuna(Zaza)