![Winner Man](https://source.boomplaymusic.com/group10/M00/04/16/64a15e259f9248efaad37b40dcaa1347_464_464.jpg)
Winner Man Lyrics
- Genre:Gospel
- Year of Release:2013
Lyrics
Yeah
Wooo
Cornerstone Muziq
Aah
Let's do this
Go
Yesu ndi one, ndipo palibe wina
Opanda iye mu gemu ndekuti palibe winner

Ndinali limodzi ndi tchimo ngati John ndi Cena
Pano mu bukhu la John akuti sindine sinner
Ndinayeletsedwa mbe ngati mkaka wokhathamira
Opanda Yesu ndithudi bwezi ine nditakamira
Anandipulumutsa, kunditulutsa mu moto
So now I don't live once like i'm yelling the motto
Chisomo chake nchodabwitsa ngati grace wam'muna
Still couldn't get it olo Chinga akhale mamuna
They think i'm mad repping Jesus koma sindinatope
Kumutsatira Jesusiyo ine sindingastope
It only makes sense to follow him and no other man
Cause nobody can change you, but Jesus surely can
Jesus surely will
And his the source of this skill
That's why without him, we wouldn't have the music to feel, let's go
Yesu ndi one, ndipo palibe wina
Opanda iye mu gemu ndekuti palibe winner
Yesu ndi one, ndipo palibe wina
Opanda iye mu gemu ndekuti palibe winner
Yesu ndi one, ndipo palibe wina
Opanda iye mu gemu ndekuti palibe winner
Yesu ndi one, ndipo palibe wina
Opanda iye mu gemu ndekuti palibe winner
Yesu ndi one
Palibe angamudrooze
Palibe angamudutse
Palibe angamusunthe
Opposition nje, palibe angamutsutse
Anamugwetsa satana palibe angamudzutse
Jesus is the winner man, he's the king of kings
Lord of the lords he exceeds all things
Mfumu ya ma fumu
Khosi ya ma khosi
Judge ya ma judge
Boss wa ma boss
Ndimanthokoza, poti anandifela pa ntanda
Anandikonda ndisanakhale olo ka khanda
Ankandidziwa kale, nde ndimangodziwa kale
Kuti sitingalekane mpakana kale kale
Yesu ndi one
Ndipo palibe wina
Olo utapanga makani, there is nobody bigger
Yesu ndi one, but he is more than a figure
His name is Jehovah Jireh
God is bigger than Jiga, let's go
Yesu ndi one, ndipo palibe wina
Opanda iye mu gemu ndekuti palibe winner
Yesu ndi one, ndipo palibe wina
Opanda iye mu gemu ndekuti palibe winner
Yesu ndi one, ndipo palibe wina
Opanda iye mu gemu ndekuti palibe winner
Yesu ndi one, ndipo palibe wina
Opanda iye mu gemu ndekuti palibe winner
Popanda Yesu mu gemu, palibe angapambane
Popanda Yesu mu program, palibe angamarane
He's running the town, palibe angamakane
Ndani angamatutse, palibe angakangane
Ndayang'ana yang'ana konse
Palibe ofanana naye Yesu
Ndi m'modzi yekhayo amene angathe
Kusintha mitima ya anthu tonse
Kuti tichire
Kuti tiyere
Palibe amene angatifele
Anitifela
Ndawomboledwa
Chifukwa cha mwazi wake wokha
Anthu amathoka
Zambirimbiri kuzipopa
But they can't live up their words but only Jesus can do it proper
Ine ndinena ndithu
Ena nambala ndi two
Amatenga namba one Yesu muzonse zinthu
He runs the game
All hands down
King on the throne man he holds that crown
Olo nditasiya kuyimba Jesusibe ndi king
Ndipo ndamaliza verse how does the hook go again?