Squad Lyrics
- Genre:Gospel
- Year of Release:2024
Lyrics
Yeah
I'm baaack
Crazy thing is
When you see me
You think it's only me
But there's more than what meets the eye
I've got a whole squad behind me
This is bigger than rap
This is ministry
This is a war
And I've got a whole army of soldiers rallying behind me
Squad
Yeah
Let's go
Chaka china tabwelanso ndi chi nyimbo
Trap sounds uwu ndi ulimbo
Fisher of men fisher of people
Call me Simon Peter when I'm preaching on the beat bro
I hope this blows up like a C4
Make an impact what I'm here for
Aiming for any one like a free throw
With the Lord's grace I might even get to three four
Ndimayenda ndi zi comfi ngati Samuel, Genda
Ndine mfana ofewa ngati Pro Gain, Mesa
Ndimanyambuta ngati Davidi
Halla muzik yanga amatitu nde iti
Akumveka ngatinso kuti ndi KBG
Koma uwu si wa Cornerstone uja
Akumvekanso ngati ndi wa Ku USA
Sound yolusa
Kodinso ndi m'busa
Ndimayenda ndi Squad
Fans yanga sungayimvetse
Ikati pa Malo ibhebetse
Ndimayenda ndi Squad
Fans yokonda prayer
Alipobe ambiri tikubwera
Ndimayenda ndi Squad
Gulu langa ndiye ndilokwiya
All the way from Nsanje to Chitipa
Ndimayenda ndi Squad
God fearing people my bro
All the same everywhere you go
Ndimayenda ndi Squad
Fans yanga sungayimvetse
Ikati pa Malo ibhebetse
Ndimayenda ndi Squad
Fans yokonda prayer
Alipobe ambiri tikubwera
Ndimayenda ndi Squad
Gulu langa ndiye ndilokwiya
All the way from Nsanje to Chitipa
Ndimayenda ndi Squad
God fearing people my bro
All the same everywhere you go
Ndimayenda ndi Squad
I'm not crazy like I'm Phronee
But I go M.A.D that's the motto
Kwina kulikonse timapita
Squad yonse imangoyipatsa Moto
I keep it 100 like I'm Jomaa
Pushing many songs like I'm Blessme
To whom it may concern like I'm Suffix
I don't do it so that you can praise me
Ndimayenda ndi chi move ngati A'Chanza
Kuphanda Li Wu ngati Still Before Da Answer
Through thick n thin I am in like Regenerate
Send me and I will go hard, delegate
Climbing higher I'ma go up, elevate
Head and not the tail that I emulate
Pokopoko paliponse the till we penetrate
Like bacteria we populate
Ndimayenda ndi Squad
Fans yanga sungayimvetse
Ikati pa Malo ibhebetse
Ndimayenda ndi Squad
Fans yokonda prayer
Alipobe ambiri tikubwera
Ndimayenda ndi Squad
Gulu langa ndiye ndilokwiya
All the way from Nsanje to Chitipa
Ndimayenda ndi Squad
God fearing people my bro
All the same everywhere you go
Ndimayenda ndi Squad
Fans yanga sungayimvetse
Ikati pa Malo ibhebetse
Ndimayenda ndi Squad
Fans yokonda prayer
Alipobe ambiri tikubwera
Ndimayenda ndi Squad
Gulu langa ndiye ndilokwiya
All the way from Nsanje to Chitipa
Ndimayenda ndi Squad
God fearing people my bro
All the same everywhere you go
Ndimayenda ndi Squad
All about free worship like I'm Chizmo
Tchimo shegu Crucked colour Echorino
Different churches everywhere but we're all fam
Izokhe! Shout out go to Ayram
I'll follow my God like Beracah
Same team winning tikumaka
Kutenga mpira mpakana Ku waka
Ma shots awo Ife tingowakha
Counting my blessings like Theresa, Phondo
Count it all joy like I'm Kelvin Sings
Thus far the Lord has brought us Ebenezer, Y.O.Y.O
If only you knew how much joy it brings
Walk in my shoes Tiya Joan
Let love lead like it's S.C.O.A.N
The list is too long I need part two
Tilipobe ambiri but we're all one
Ndimayenda ndi Squad
Fans yanga sungayimvetse
Ikati pa Malo ibhebetse
Ndimayenda ndi Squad
Fans yokonda prayer
Alipobe ambiri tikubwera
Ndimayenda ndi Squad
Gulu langa ndiye ndilokwiya
All the way from Nsanje to Chitipa
Ndimayenda ndi Squad
God fearing people my bro
All the same everywhere you go
Ndimayenda ndi Squad
Fans yanga sungayimvetse
Ikati pa Malo ibhebetse
Ndimayenda ndi Squad
Fans yokonda prayer
Alipobe ambiri tikubwera
Ndimayenda ndi Squad
Gulu langa ndiye ndilokwiya
All the way from Nsanje to Chitipa
Ndimayenda ndi Squad
God fearing people my bro
All the same everywhere you go
Ndimayenda ndi Squad