
Shegu ft. EchoRino & Crucked Color Lyrics
- Genre:Gospel
- Year of Release:2020
Lyrics
Mmmmm
Highly underrated
Yeah, ih, koma
TNO
Echorino
Crucked Color
Ndinapenga kale ka
Ine toto, kumwa mowa
Ili ndipangano lomwe ndinalowa
Bola sobo, ndikakondwa
Kutchilla ndi ma members tonse tili sober
Ati "iwe TNO ukufuna utinamize?
Mowa ungakane titati tikulawitse?"
Eya ine shegu izo nkumanzere
Mayesero akabwera ife timangotere
It goes like one, two, three and to the four
Push temptations away when they creeping through the door
Five, six, seven to the eight
You can sing along if you feel like you relate
Mayesero angongobwera ife timati
Shegu
Tchimo lingatchene bwanji ifeyo
Shegu
Mawonekedwe amapusisa uziti
Shegu
We don't do that around here
Shegu
Wati bwa?
Shegu-shegu
Shegu-shegu
Shegu-shegu
Shegu-shegu
Shegu-shegu
Shegu-shegu
Shegu-shegu
Shegu-shegu
Echo kanazi aka! (Shegu)
Hhm kabawa nanga? (Shegu)
Ma baby awa? (Shegu)
Inu ndiye Kaya amwene ndinu trad
Eeh, inedi ndine trad
Ndichifukwa chake zachigulugulu simpangadi
Ndinapanga chisankho
Chotsatila m'modzi
M'modzi yemweyo anamangilira khosi sindicheukira tchimo
Sine otengeka sindimadyela kunthiko
Kubwera kwachisomo kunachotsa zikhomo
Kodi simudabwa ndikamuvunga chi elbow?
Awuze amvetse
Eh, ndili ndi Yesu man
Kachasu ndim'dani sitimvana man
Mary-jane tidana sabweraso kwathu
Osamandiyesa siine wamba munthu
Pano ndine Minister shegu
Yesero kubwera ili (Shegu)
Mukakapopa katchimo still (Shegu)
Shegu aaah!
Mayesero angongobweras ife timati
Shegu
Tchimo lingatchene bwanji ifeyo
Shegu
Mawonekedwe amapusisa uziti
Shegu
We don't do that around here
Shegu
Wati bwa?
Shegu-shegu
Shegu-shegu
Shegu-shegu
Shegu-shegu
Shegu-shegu
Shegu-shegu
Shegu-shegu
Shegu-shegu
Aaah iwe, Crucked, right up!
Osapezeka pa kati-kati pamoyo ndi imfa
Ndi angati-ngati amvetsela ndiyimba
Zimayamba mocheza aku kodola
Eko Five hands ndiwe nfana otsogola
Akusungila ka mpeni kumphasa
Akufuna moyo wako iwe uwuona ngat mphasha
Sutha kukana bwanji
Paliponse ufunthepo bwanji
Sheeeegu
Mabodza onse uko
Timowa tonse uko
Sheeeegu
Kubanda konse uko
Minyama yonse uko
Turn your lights on
Ndiwe kuwala
Angaku kope za Yesu osaiwala
Ena adza tsala popita kumwamba
Ukapanga zunguli zunguli pama kwerelo udza tsala
Shegu udzimu mvetsetsa
Palibe okuletsetsa
Mayesero angongobweras ife timati
Shegu
Tchimo lingatchene bwanji ifeyo
Shegu
Mawonekedwe amapusisa uziti
Shegu
We don't do that around here
Shegu
Wati bwa?
Shegu-shegu
Shegu-shegu
Shegu-shegu
Shegu-shegu
Shegu-shegu
Shegu-shegu
Shegu-shegu
Shegu-shegu