Mundikumbutse ft. Gwamba Lyrics
- Genre:Others
- Year of Release:2022
Lyrics
Ritaa
Sispence
Kukhululuka, monga momwe inu muchitira (forgiving just like you do)
Kukonda, olo adani momwe mufunira (Loving, even enemies just as you wish)
Ndipo ndikasochera, kwa inu mundikokera (and when I stray, you pull me back to you)
Mundigwire mkono, mundimenyera Nkhondo (hold my hand, you fight my battles)
Ndikumbuke maumboni ( let me remember the testimonies)
Ndipo ndikuyamikeni (and let me thank you)
Ngakhale pamavuto, ndikulambireni ndikutamandeni
(Even when am troubled, let me worship you, praise you)
Mundikumbutse (remind me)
Kuti Moyo wanga udalira inuyo (that my life depends on you)
Mundikumbutse (remind me)
Komwe ndachoka podalira inuyo (how far I've come, by depending on you)
Mundikumbutse
Mundikumbutse (remind me)
Yo, pena ndimafila ngati ndili ndekha
Kuyesa kuphusha ngini koma osatheka
Ndikuwe bwanji, mwina poti sizikumveka
Koma ndikakumbuka mawu anu ndimadekha
Inu munati munditsegulira ndikagogoda
Ndikadwala nde mumasanduka dokota
Nde satana amabwera ndikutokota
Koma pamtima panga munaika loko ka
Inu ndinu alpha, omega
Kundikonda mpaka ndzafa, osaleka
Nde mavuto akabwera sindilira
Ndimayang'ana kwa yahweh,
Ndimadziwa kuti sanganditaye