Smoko ft. Jay Jay Cee Mw Lyrics
- Genre:Others
- Year of Release:2024
Lyrics
Ooohh
Ay ay ay ay ay
Ritaa, Sispence
And aJay once again, Stradamus
Ndakukonda koma ndamva kuti ndiwe smoko
Akuti mbiri yako ndiyakuda kuchita kuposa Coco
Boy ngati wandikonda konda bwanji ukumvera anzako
Angofuna akunamize, ine samandidziwa choncho
Akuti ndiwe kadzidzi
umayenda usiku, dolo wa izizi
Khazika mtima pansi am a good girl
Usathamange magazine
Baby mantha, mantha mtima mantha
Usachite mantha, mantha iwe mantha
Akuti Smoko iwe, smoko
Ai si smoko ine, smoko
Akuti Smoko iwe, smoko
Ai si smoko ine, smoko
Akuti Smoko iwe, smoko
Ai si smoko ine, smoko
Akuti Smoko iwe, smoko
Ai si smoko ine, smoko
Ati umaposa ma diva apa video
Ndikapusa adzandimva pa radio
Pa ma uthenga achisoni, ati iwo ali ndi mboni
Sine oyera, nkhani zambiri amangondipekera
Sindili innocent ai
Koma ndzakukonda till the day I die
Baby mantha, mantha mtima mantha
Usachite mantha, mantha iwe mantha
Akuti Smoko iwe, smoko
Ai si smoko ine, smoko
Akuti Smoko iwe, smoko
Ai si smoko ine, smoko
Akuti Smoko iwe, smoko
Ai si smoko ine, smoko
Akuti Smoko iwe, smoko
Ai si smoko ine, smoko