Wa Ine ft. Leslie Lyrics
- Genre:Electronic
- Year of Release:2021
Lyrics
Hmmm Leslie
Yea yea yeah, Ritaa
Kodi ndi ndani?
Ukuimba foni ukufuna chani?
Ukuti ndimusiye
Ukukamba zosatheka
Zoti undiopseza zokhazo sizitheka
Iweyo ndi ndani?
Umamuimbira foni ngati ndani?
Ukuzitaitsa nthawi
Kunyumba kwanga nkomwe iye ali
Amakonda tachitsikana
Anzako anandiuza
Ndimampatsa zomwe amafuna
Ndine amene amafuna
Ndimampatsa zomwe amafuna
Ndine amene amafuna
Uyu ndi wa ine, wa ine, wa ine
Uyu ndi wa ine, wa ine, wa ine
Uyu ndi wa ine, wa ine, wa ine
Uyu ndi wa ine, wa ine, wa ine
Uyu ndi wa ine, wa ine, wa ine
Uyu ndi wa ine, wa ine, wa ine
Akamabisa foni
Sudabwa iwe eh eh?
Adzakusiya
Akadzangotopa nawe eh eh
Phokoso la Chule
Sililetsa ng'ombe kumwa madzi
Lero ali ndi iwe, Mawa ali ndi ine
Ndi m'mene zinthu zikhalire
Amakonda mkazi wangwiro
Anzako anakunamiza
Ndimampatsa zomwe amafuna
Kukutaitsa Nthawi nzomwe akufuna
Ndimampatsa zomwe amafuna
Kukutaitsa Nthawi nzomwe akufuna
Uyu ndi wa ine, wa ine, wa ine
Uyu ndi wa ine, wa ine, wa ine
Uyu ndi wa ine, wa ine, wa ine
Uyu ndi wa ine, wa ine, wa ine
Uyu ndi wa ine, wa ine, wa ine
Uyu ndi wa ine, wa ine, wa ine
Ndithana nawe, nawe, musiye
Ndithana nawe, nawe, ndisiye
Uyu ndi wa ine, wa ine, wa ine
Uyu ndi wa ine, wa ine, wa ine
Uyu ndi wa ine, wa ine, wa ine
Uyu ndi wa ine, wa ine, wa ine
Uyu ndi wa ine, wa ine, wa ine
Uyu ndi wa ine, wa ine, wa ine