
CHETE CHETE ft. Martse Lyrics
- Genre:Hip Hop & Rap
- Year of Release:2022
Lyrics
Ndausa nyama no chete Chete
Ndimatha kuimba sindi dalila kethe kethe
Ndadusamo katatu mwanjovu
Mpheche mpheche
Ukandilakwira nde Bwera upepese
Ndina bwera mu Game ndizi phokoso
Ndipo ndalimbamo ngati nkhuku ya lokolo
Pokopoko Martse Martse ndi chi dolo
Kwasalaku ndizilipilisa msonko oho
Ulemu upitenso kwaine ndemwe
Chisomo cha Mulungu sichinandi semphe yeah
Chete chete sausa nyama
Chonde osama namizana mafana
Ndimango wona mukamakamba
Chonde osama namizana mafana
Eniyake Martse afika adzah
Eniyake Martse afika adzah
Eniyake Martse afika adzah
Aaaa aaa aah
Ndikulandila ma flowers anga ndili moyo
Sindili panja ndili momo wamva Mymo uh
Couldn't even be starve by the Bobo
They never lied to you
Am very very unsocial
Komabe uzandipeza ndili clab ndili phee
Ndikayamba kuyakha undiona ndi mwe
Ndi kamkadzi koyera kali mbeee
Olo akhale black beauty bola ali chweee iwe
Ulemu upitenso kwaine ndemwe
Chisomo cha Mulungu sichinandi semphe yeah
Ulemu upitenso kwaine ndemwe
Chisomo cha Mulungu sichinandi semphe yeah
Chete chete sausa nyama
Chonde osama namizana mafana
Ndimango wona mukamakamba
Chonde osama namizana mafana
Eniyake Martse afika adzah
Eniyake Martse afika adzah
Eniyake Martse afika adzah
Aaa aaa aah
Chete chete sausa nyama
Chonde osama namizana mafana
Ndimango wona mukamakamba
Chonde osama namizana mafana
Eniyake Martse afika adzah
Eniyake Martse afika adzah
Eniyake Martse afika adzah Aaaaaaah