![Mantha](https://source.boomplaymusic.com/group10/M00/07/24/4342f77cf5a54fc9ab686df31bfb0c6d_464_464.jpg)
Mantha Lyrics
- Genre:Others
- Year of Release:2022
Lyrics
Ooowh ooowh oohw
Yeee yeee
Ndili ndimantha undiuza mtimau
Sungazimvetse kunena ndimau
Ndipite kwanu iwe upite kwathu
Mwina kwathuko ukapezako zitatu
Ndinvetsetse ulimbe nane
Usadule Chikondi chaine ichi
Wakulila pizza iwe sungaliziwe denje
Siunauwoneko umphawi wozama dzenje
Despite for my poverty timbili tonyasatii
Will you still lo lo lo love me
Despite for my poverty timbili tonyasatii
Will you still lo lo lo love me
Oyeee
Ndili ndimantha mantha mantha ine iih
Ndili ndimantha mantha mantha ine
Ndili ndimantha mantha mantha ine
Abale ako ndinamva ndi ageri
Ine sukulu-yo certificate ya eight
Kodi nyumba ya udzu yopanda wi-fi
Ungakhalemo iwe ungagonemo iwee?
Umaonamo chani mwaine
That you even willing to change your Name for me
Wakulila pizza iwe sungaliziwe denje
Siunauwoneko umphawi wozama dzenje
Despite for my poverty timbili tonyasatii
Will you still lo lo lo love me
Despite for my poverty timbili tonyasatii
. Will you still lo lo lo love me
Oyeee
Ndili ndimantha mantha mantha ineyo
Ndili ndimantha mantha mantha ine
Ndili ndimantha mantha mantha ine
Ndili ndimantha mantha mantha ine
Umaonamo chani mwaine
That you even willing to change your Name for me
Don't change Nooo
Dispite for my poverty
Don't change ooh
Mbili yo nyasa don't change Noo
Dispite for my poverty
Timbili tonyasa