
24hrs Lyrics
- Genre:Soul
- Year of Release:2023
Lyrics
24hrs
Awo akuti chikondi chinathaa
Anthu panopa akumanamizana
Akut true love kulibee
Ukagwa mchikondi ulimbee
Why why why?
Look into my eyes
Say it to my face
Ungandiswele mtima iwe
Tsiku limoodzi?
You Should Look into my eyes
Say it to my face
Ungandiswele mtima iwe
Tsiku limoodzi ine?
Osasiyana
(24 hrs ..limodzi)
Ma phone othimaa
(24 hrs ..limodzi)
Ukhale wa inee ee
Love yopanda malile
Ukhale ndi ine eee
(24 hrs ..limodzi)
Long term love.. anakunamizapo
Ukufuna za mpaka muyaya ena anakupusisa kuchinsapo
Wati sumafunaso kukonda ..chikondi kulibe
Love me kwa tsiku limodzi
Zodandaula kulibe
Moti kwatsiku limodzi ndinga kucheate inee?
Tsiku limodzi ine ndingaone pena?
Tsiku limodzi inee ndingatope nawe?
Moot ungepeze ndapanaa?
Tsiku limooodzi
Osasiyana
(24 hrs ..limodzi)
Ma phone othimaa
(24 hrs ..limodzi)
Ukhale wa inee ee
Love me opanda malile
Ukhale ndi ine eee
(24 hrs ..limodzi)
Moyo ndikamodzi... Zolilitsanazi njee
Moyo ndikamozi .. Zokakamizazi njee
Ndikonde kwa tsiku limozi..wako ndikhale ndekha
Ndikukonde kwa tsiku limodzii
Osasiyana
(24 hrs ..limodzi)
Ma phone othimaa
(24 hrs ..limodzi)
Ukhale wa inee ee
Love yopanda malile
Ukhale ndi ine eee
(24 hrs ..limodzi)