![Mundiuzeko ft. BEE JAY, Ace Jizzy & VUBE](https://source.boomplaymusic.com/group10/M00/09/21/04853a652a0a4729a707fedc7ea902aeH3000W3000_464_464.jpg)
Mundiuzeko ft. BEE JAY, Ace Jizzy & VUBE Lyrics
- Genre:Hip Hop & Rap
- Year of Release:2021
Lyrics
Mundiuzeko ft. BEE JAY, Ace Jizzy & VUBE - Guntolah
...
louder! !! komaaa, guntola iweo..
beee jayy, iii, vubee (ndathana nazo izi)
mfana waukape iwe
uli ndi moyo waukazitape mphwanga
uwona chomwe chinameta phanke nkhanga
ma default, ubwerera pomwe unali before bee
ndinakupatsa last chance,
ndikudabwa jizzy akundiuza mukuvayisana
awa nthawi tangotaisanaaso
ndimaona ngati ndili mu Chikondi
koma rhoda, nkhani yocheza awiri umamwaza kwa fanz boarder
ndili ndi may amozi, uzimwa bufen frust yako ukagobagoba.
chorus
ngat akazi onsewoo,
Ali ndi moyo ogona ndi amuna onsewoo,
ngat chilungamo chimawasowa, nde kuti chikondi sichiliso mwaiowa.
ndewa wabwino mukampezako, chonde ndikupepha mundiuzekooo. x2
kodii, ndisacheze nanu? nkhani ndisakambe nanu? mpaka nzanu aziziwe nanu?
bas ndingothana nanu