Amacheza ft. Charisma Lyrics
- Genre:Hip Hop & Rap
- Year of Release:2022
Lyrics
Louder koma guntolah iweyoo
Chariz
Madolo amacheza okhaokha
Mbava zimacheza zokhazokha
Mahule amacheza okha okha
Nawo ma kape uwapeza kucheza okha okha
Muone nzakoyo muone nzakoyo
Muone nzakoyo muone nzakoyo
Muone nzakoyo muone nzakoyo
Muone nzakoyo muone
Malawi kudana tokhatokha
Zabwino apeze okha okha
Kupeza mavuto tiziwa ndalama akapeza kugawana okha okha
Mayo ndima ras, no
Rambo ndi khilishina
Nkango ndi fisi
Nambe ndi Chrissy
Nkango ndi fisi yayi
Dyabu ndi oukila sungampeze akuyenda za moyo zinayi
Nkhuku ndi fish sungazipeze
Kusanja ma plan zitakhala busy yea
Asazakunamize, nzanga ndi hule ine ndi sisteli
I don't kiss and tell osangokhala bwanji osamu kissa
Gin ndi spirit how munthu okufa kumwesa osaukisa
Ena thukuta osali khesa
Kupeza ndalama osazi chaser
Kuthela mowa osau chaser
Ndalama hule osaonkhesa zitanchulukila
Madolo amacheza okhaokha
Mbava zimacheza zokhazokha
Mahule amacheza okha okha
Nawo ma kape uwapeza kucheza okha okha
Muone nzakoyo muone nzakoyo
Muone nzakoyo muone nzakoyo
Muone nzakoyo muone nzakoyo
Muone nzakoyo muone
Malawi kudana tokhatokha
Zabwino apeze okha okha
Kupeza mavuto tiziwa ndalama akaleza kugawana okha okha
Anali nzathu asanakule
Nzathu asanaphule
Tinkamvala kale asanamale
Pano ati ena anamata kale
Sangapange fodya anansiila Barry Uno
T-shirt ya Bob Marley kuno
Suzandipeza ndi kucheza ndimakape
Ndimaziwa anthu ambili mumafuna kumacheza nane
Sine size yanu we not the same
Ten years now I've been in the game
I've been killing em they know my name
Never flopped I stayed in my lane
Shooting star am a superstar
Udolo wanga umachita kuoneka
Namenya lit ndimamenya ma hit
Mupange quit
Apo bwi mutha mpwiti
Dzuwa salodzelana sipanga nao zibwana
Ndalama bwee pwamwamwa
Am in my own lane u can not contain
Am in that top 10
Inu muli pa mpeni
Madolo amacheza okhaokha
Mbava zimacheza zokhazokha
Mahule amacheza okha okha
Nawo ma kape uwapeza kucheza okha okha
Muone nzakoyo muone nzakoyo
Muone nzakoyo muone nzakoyo
Muone nzakoyo muone nzakoyo
Muone nzakoyo muone
Malawi kudana tokhatokha
Zabwino apeze okha okha
Kupeza mavuto tiziwa ndalama akaleza kugawana okha okha