![Ndatopa ft. K Banton](https://source.boomplaymusic.com/group10/M00/09/21/2fa4656c0a1e43d3a4ef8f6d4b3e2ecaH3000W3000_464_464.jpg)
Ndatopa ft. K Banton Lyrics
- Genre:Hip Hop & Rap
- Year of Release:2019
Lyrics
Ndatopa ft. K Banton - Guntolah
...
Guntola x k banton
mmmmh yah woza.. k banton
louder.. koma guntola iweyo
K BANTON
ndatopa nazo zomati mukandihala pa app Mose mwayambila kd iwe ase ukuta?
ndatopa nazo zomati mukandiona mu nsewu mupemphe bas kadora kanga ndimakhala ndakhetsa thukuta
tauser po Dora ndikukanika ma Toro
ndikupanga ngini upload kumakanika ma award
nde ndikunenetsa
ndimapanga zanga zanga mboni yanga piksy
pano ndutha zaka zaka mboni yanga Jimmy
at wanenepa heavy ukufunika gym et
man ndizingokhala ndimene ndililimu et
amzanga panopa Ndi ma # wooh
nyimbo itha kukhala lebo wooh
kucheza pano akudisa lero wooh
ndatopa nazo zomati bredah yooh
kucheza wooh yeah wooh
GUNTOLA
Plz plz be humble yeah, plz plz aah mzabhobho
at beat nkajampira aaah mzabhobho
luso ngat naija Ndi la popo, aki
at chibuku chili park
ma ex ma reback
chufuna malidadi
ankalesa ndinkat azapusa sinat
ndizasamutsa ghettoh kusamutsa ngat gati
aaaaaah
zanga zinaera mfuse banton
hater ndasiya kumpazi mfuse batto
batty bwai, use wayi ndatopa, mfuse waly
aah dona siyisowa, dola zikandisowa
is a your chick simple one
listen, simple by or you need that I can do high
timuone mwina undipatse candle
undipeze Pendle
undipatse mwendo wapazanja sindilora
Pali zifukwa zomwe ndimapanga
Pali zifukwa tangoganiza
Kaya ndinatha ndimapanga zanga
osandiputa chonde chonde
Ndatopa, ndatopa
ndatopa, ndatopa
ndatopa, ndatopa
ndatopa, ndatopa
woza, yeah
woza bwera nde titenge chithunzi
flashlight pasakhale chinthunzi
ndatopa nazo man, zilowa hustle man
pin chithunzi
mboni Ndi gunto man kapena rival Shan
zimandikhudza
everyday we ganna make a little goal
nyamata nzanga mpakana video call
ase what are you doing and never what your business kd
kundilonda kulikonse nditapiteko
What's up ghetto boy I'm hard like metal
ndi natopa heavy yeah I'm from ghetto
mission, never move from stable
black black yeah still black like table
ndili free pa den aku ndipanga follow
ndi natopa ndi zovala nditadziwa solo
ndungogwetsa Zi ma bars singakhale cell
ndili under-arrest mzuli premo
ukamufumse nkasayo, ndatopa nazo usanditchule at bwa ntasayo
ndatopa nazo Zama stant siinu Bruce Lee
umburi watopetsa osangodya peace
nkaz wako ndantuluka kulowa Bc
koma weyo banton ndinu afisi wooh
( we got deh hyena)
ndatopa nazo zakupatsa blow zonditchura bro
uli ma hope
ndikufuna nzaku marry hiho hiho
(hiho hiho)
Pali zifukwa zomwe ndimapanga
Pali zifukwa tangoganiza
Kaya ndinatha ndimapanga zanga
osandiputa chonde chonde
ndatopa ndatopa
(aaah umandihala plug)
ndatopa ndatopa
(aaah aah aah aah)
ndatopa ndatopa
ndatopa ndatopa