Kodi ? (Alternative Version) Lyrics
- Genre:Others
- Year of Release:2022
Lyrics
DJ ndiyambe?
Okay
Tellem ah
Okay
Listen up ya
Brah
Kodi (Ehe)
Mukamayankhula mumaganizila pa mawa Kodi (Funso)
Mukamatinena mumayesa sitimamva Kodi (Inu)
Mumaona ngati zinthu zanu nza muyaya Kodi (Bwana)
Zoti dziko lino limasintha munayiwala Kodi?
Kodi, bwana Kodi
Mumayesa Monday ndi Sunday
Kodi Kodi afana Kodi
Mphatso ya Jah Jah mungalande
Kodi, Kodi bwana Kodi
Mwala wapa ngodya mungakankhe
Kodi Kodi ntchana Kodi
Tsiku la forty mungasankhe
Kodi asisi Kodi
Do you know nsanje ndi ufiti Kodi
Lady makes cash nde ndi busy body
You gon stay like that while busy loading
You busy holding
Meetings just to roast and beef your buddies
Only God knows tili ndi migodi
Tsiku ndili modzi Bola pin code
(Nkasa Ase Bola pin code)
Inde ngati phungu man
Better talk from afar sife a khungu man
Za mtsogolo amaziwa ndi Mulungu man osati munthu man
Zabobo some day tizakutulukani
Tikapeza money tizakukumbusani
Tili nyumba zanu
Tinali nkhumba zanu
Mumaganizila ngati za tsogolo lanu hah
Kodi
Mukamayankhula mumaganizila pa mawa Kodi (Funso)
Mukamatinena mumayesa sitimamva Kodi (Inu)
Mumaona ngati zinthu zanu nza muyaya Kodi (Bwana)
Zoti dziko lino limasintha munayiwala Kodi?
Kodi, bwana Kodi
Mumayesa Monday ndi Sunday
Kodi Kodi afana Kodi
Mphatso ya Jah Jah mungalande
Kodi, Kodi bwana Kodi
Mwala wapa ngodya mungakankhe
Kodi Kodi ntchana Kodi
Tsiku la forty mungasankhe
Is it so
You didn't know
Zoti chalo Chino ndingati pa dancefloor
Ukavinavina palowa anzako
Life moves fast and then in slow Mo
It's a game of turns nza after domo
And when you stay humble it seems so normal
You meet zikhomo
Maluzi mono
Just stick to your goal
You'll pass it all bro
Ndeno Breda imva uphungu one
Keep your enemy close if you know them son
They'll be sticking their nose in your business man
Don't be foolish fam
Just watch them run
Nzabobo someday azakutulukani
Ukapeza Monday azakukumbusani
Muli pa chi nzanu sanali mbali Yanu
Amaganizila ngati za tsogolo lanu
Hah