![Chasintha Nchani ? ft. Nonymous Mw](https://source.boomplaymusic.com/group10/M00/07/29/0705842930e244be8fcb7a07ab79e4a7_464_464.jpg)
Chasintha Nchani ? ft. Nonymous Mw Lyrics
- Genre:Others
- Year of Release:2022
Lyrics
Yeyeyeye
Zonse zomwe ndinakuchitila
Takumbukila ndinakupangila
Za mu mtima mwangamu ndithu
Koma iwe sunkandimvetsetsa
Nthawi zonse ndikakuyankhula
Unkangowona ngati nzocheza
Akwanu ankakufunsa
Anzako ankatidabwa ah
Unkawayankha kuti
Ndimakuvutisa
Ndinati koma eh eh
Koma asisi
Musandinyozese
Mwina tizingocheza bwa
Mesa unkandisizer
Unkati ndachepa nazo
Mesa sunkandifuna iwe
Unkanditchula nchimwene eh
Ndeno
Chasintha Nchani Judie
Sunkandimvera Judie
Sunkandifuna Judie
Ndeno usandibalalitse
Chasintha Nchani Judie
Ndikayimba phone Judie
Unkandidula Judie
Mesa unkati uli busy
Oh noh noh noh noh
Ndeno Chasintha Nchani Judie
Oh yeah yeah yeah
Mesa unkati uli busy
Oh noh noh noh
Chasintha Nchani Judie
Oh yeah yeah yeah
Mesa unkati uli busy
Ine ndine odekha
Mtima wanga woleza
Zachikondi naleka
Poti Pano ndinagiver
Mpomwe iwe ukubwera
Kumafuna kundiyesa
ATI bwanji siticheza
Mesa Kodi ndinafwifwa
You gave me your heart I sent it back
Wasted your time I want it now
Chilichonse chomwe nakuchitila
Sunkachifuna
Vuto si iwe
Vuto ndine pomakomedwa
Usakonde munthu
Kuposa Mene akukondela
Oh ndinkakusizer
Nkati wachepa nazo
Ine sinkakufuna
Nkakutchula kuti nchimwene
Oh ndinkakusizer
Nkati wachepa nazo
Mesa sinkakufuna
ndinkakutchula nchimwene
Chasintha Nchani Judie
Sunkandimvera Judie
Sunkandifuna Judie
Ndeno usandibalalitse
Chasintha Nchani Judie
Ndikayimba phone Judie
Unkandidula Judie
Mesa unkati uli busy
Oh noh noh noh noh
Ndeno Chasintha Nchani Judie
Oh yeah yeah yeah
Mesa unkati uli busy
Oh noh noh noh
Chasintha Nchani Judie
Oh yeah yeah yeah
Mesa unkati uli busy
Busy yeah