IMA KAYE Lyrics
- Genre:Others
- Year of Release:2023
Lyrics
One of a kind
Zakazi ena baby I'm so blind
So hard to find
Kukula nawe ndithu I wouldn't mind
Umandiwaza
Zochitika zako nzofasaaaa
Mkazi wanga yi
Ndithu CHAUTA uyu anapanga
Beautiful woman
Pa iweyo ndingasinthe chani
Mkazi wowala ndi mtima momwe
Ndimubise bwanji
Beautiful woman
Pa iweyo ndingasinthe chani
Mkazi wowala ndi mtima momwe
Ndimubise bwanji
Ima Kaye eh
Kaye eh
Mpheteyi uyivale eh
Vale eya
Ima Kaye eh
Kaye eh
bwera ndiku marry eh
Marry eya
Funsa asisi
Ndili nchikondi chozaza peace
Kumva kukoma ndili pa ease
Bwera pafupi nkupatse kiss mwaa
Funsa a chimwene
Ndikumayenda nditazazidwa ndi chimwemwe
Nyengo ya Mvula wayisundasusa chilimwe
Nde mundilole kuti leroli ndisimbwe eh
Beautiful woman
Pa iweyo ndingasinthe chani
Mkazi wowala ndi mtima momwe
Ndimubise bwanji
Beautiful woman
Pa iweyo ndingasinthe chani
Mkazi wowala ndi mtima momwe
Ndimubise bwanji
Ima Kaye eh
Kaye eh
Mphete uyivale eh
Vale eya
Ima Kaye eh
Kaye eh
bwera ndiku marry eh
Marry eya