Njala (feat. Lanji) Lyrics
- Genre:Afrobeats
- Year of Release:2021
Lyrics
Njala ft. Lanji - Goddy Zambia
...
ne nibakonda alume angu nawo onikonda bavitikkila banja yasu kuti tisakafe nanjala-a-a mwapeza ncito kukalale pemwenze luta mwenzeti mukaweele nomba papita matsiku manyinjiii bana balila njala ne nibape cinji.
njala*5 mukkawele liti*2
kuno mind you nabbwelela zancito koma zonse zili kuno kulibbe tincito ndinadikila kufikila zakulya zonse ndinatenga zinataa panjila ndalama zinagwa k20 ndinasala nayoyo inataaa ndingatumiza koma k10 ndiyo ningasala nayo nizayesesa kukongola kwaanzanga but ndikacelwa nditumiza osadanda nimagoko ndikumenya kuno ndiyanzanga zikakwana zokkwelela ine ndizajika kufika kujika kufika kujika kwatu ukongo kufika kujika Kongo ndizafika kujika kufika kujika kwatu ukongo kufika kujika Kongo
njala*5 mukkawele liti*2
ana Ali bwanji ndinu mulibwanji agogo mukukkala nawo kondi mulibwanji eee mukawone amake dalitso kuli comwe ndatumiza Kongo kuli mabvuto mufa njala ana njala ati mbuto zyakubyala munadya ciwaya eee ija nkongole anatenga Sabina inito andiuza sanalete sarafinaaa njala*4 ndiziba mukufa njala koma ndikubbwela mukumo osacedwa
njala(njala)*5 mukkawele liti*2
njala aaa njala mukkawele liti
njala hee njala aaah mukaweele litiiii
muzafika kujika kufika kujika kwatu Kongo kufika kujika Kongo*2
njala *4 ooh njaa-a-a-a mukkawele liti