Sakukonda ft. Yo Maps Lyrics
- Genre:Afropop
- Year of Release:2023
Lyrics
Sakukonda ft. Yo Maps - Goddy Zambia
...
CHORUS (YO MAPS)
Umankala Che okwiya
Sakusunga mushe my dear
Better you find someone who loves you
Okukonda namutima onse baby
Vi ipilako day by day
Amakumenya everyday
Sakukonda anyway
But umukonda so chabe
Umankala Che okwiya
Sakusunga mushe my dear
Better you find someone who loves you
Okukonda namutima onse baby.
VERSE 1 GODDY ZAMBIA
Kuli ntawi yene ungatichite vene mutima wako umafuna
Kuliko futi ntawi yene bantu bamamvela vene umalila
Osazigong’a baby ayo Nimavuto vuto
Koma anzanu sibakhala so kukhalila mkangano
Oh yah yah yeh!
Langa chongo ndiye nkani
Ku fighter daily ndiye nkani
Longa zakozo yendani
Akhozatu kukhuphani
Ye iye
Anayambala khale panopa sungakhale
Mwayesa mwayesa zakanga
Zika kanga sakakamiza
CHORUS ( YO MAPS)
Vi ipilako day by day
Amakumenya everyday
Sakukonda anyway
But umukonda so chabe
Umankala Che okwiya
Sakusunga mushe my dear
Better you find someone who loves you
Okukonda namutima onse baby.
VERSE 2 (GODDY ZAMBIA )
Saku samalila
Samadziwa mokhalalira
Uli ndwii ndwii Akudoba
Amafuna potawira
Aku kalipila amafuna poyendela
Nzelu zake zonse samangoku ganizila
Sikuti ndikufuna ndine
Ndiri modzi wa iwo amakumvera Iwe
Kenaka maka maka ine
Misozi zako zatika mokanga ndipo
Chikondi koma makondedwe
Dzulo munakanganatu pama kambidwe
Chemwali osazipanga eh eh eh
Kutawa zikawawa eh eh eh
CHORUS (YO MAPS)
Umankala Che okwiya
Sakusunga mushe my dear
Better you find someone who loves you
Okukonda namutima onse baby
Vi ipilako day by day
Amakumenya everyday
Sakukonda anyway
But umukonda so chabe
Umankala Che okwiya
Sakusunga mushe my dear
Better you find someone who loves you
Okukonda namutima onse baby.