Could have been better (feat. Neo Slayer Zambia) Lyrics
- Genre:Afrobeats
- Year of Release:2021
Lyrics
(Chorus neo)
Izi misozi nalilapo ma years
Nayeve iyi ni time naonongapo pokupeza
( Ah ya ya ya )
Iyi love napasapo ba wrong
It could've been sweet memories si story no
It could have been better
(Nga kwenze map)
It could have been better
(Yokupezelapo)
Ngati okukonda enzo badwa na zina yako
Pachalo (X2)
VERSE 1
Imagine to skip even your first heart break
Sembe pano sitiviziba vama heart break
Ngati kunali mwana abadwa alila zina
Yaokondedwa wache zingapangise sense
Imagine kusamenyana cifukwa chosaziwana
Imagine kusakaniwa cifukwa sinu okongola
Imagine kusa ima mjila
Kutaya ntawi yofuna muntu
Mene suza khala naye nthawi
Kupanga malonjezo mene simugwira
Muli mucikondi koma iye achiting'a
Kupanga ma effort maganizo yachi kwati
Kansi iyi aganizila kuku using'a
Panotu sindidziwa zoona
Kukonda muntu mosadwiwa
Sadziwika amene ndili naye ngati ndiwa zoona
VERSE2
Ndikakumbukira misozi zinatika
Mutima anan'gamba mutima ndina menda
Anau ononganso
Ndikakumbukira mutima umawawa
Popeza okukonda ndiku pita mosa pita
Kufuna osafuna
Sometimes ungamve ngati wakondedwatu
Mosadziwa kansi upunzila mokondeladi
Ungatenge nkazi amene sayenera
Cifukwa chofela nkope basi mwakwatilana
I wish kunalibe ndi ex wanga
Tina siyana ananipasa che kamwana
Kwenze kudala pano niyenda nawinango animvesa ulesi nifunanso winango