Sendera Lyrics
- Genre:R&B
- Year of Release:2020
Lyrics
Sendera - Quest MW
...
Quest_Sendera
Yaah
Mtima mwanga zimafunso zili mbwee yaah
Ndizikhala bwanji ndekha
Kuyambira tsiku lomwe unandileka
Moyo mwanga sizikutheka
Nzovuta kuyiwara tima memories yaah
Utabwelera moyomu nde ndinga file victorie ih ah
Ndizolowere munthu wina
Ine singakwanise kapena nfuse iwe mwina ah yah
Ndizicheza ndi wina
Ine singakwanise kut ndi kawoneso wina
Ndikupempha sendera
Mtima mwanga unakweza mbendera ah yah
Umandiwaza ukasekelera ah
Nkomwe mtima wanga unathera
Sendera pafupi fupi fupi fupi
(Sendera)
Sendera pafupi fupi fupi fupi
(Sendera)
Sendera pafupi
Thupi langa limandiuza lasowa lako thupi
Achibale amandifunsa
Ukuyenda bwanj wekha mensa munkayenda 2ppo
Nali munthu ine nde chifukwa cha iwe
Mavuto nde nkayiwala chifukwa cha iwe
Ndasowa okhala nawe limodzi nde tiyetu bei
Chikondi chako nde chinalibe holiday
Ngati zili zotheka beb am sorry am sorry am sorry am sorry
Sindizabwerenzaso zikhani ma story ma story ma story ma story
Beb give me one chance eh
All I need is one dance eeh
Ndikufuna moyo mwanga
Ndiyambireso ku njanja
Ndikupempha sendera
Mtima mwanga unakweza mbendera ah yah
Umandiwaza ukasekelera ah
Nkomwe mtima wanga unathera
Sendera pafupi fupi fupi fupi
(Sendera)
Sendera pafupi fupi fupi fupi
(Sendera)
The End
Aux