
Malawi Lyrics
- Genre:R&B
- Year of Release:2020
Lyrics
Malawi - Quest MW
...
Mm-mm-mm
Yah, yeah, eh, eh, eh
Yeah, eh, eh
Mm-mm-mm (Loyal- loyal hustle the factory)
Eh-yah, Quest
Malawi
Ndikuwoneko
Ndikuwoneko (mm, hmm)
Malawi
Ndikuwoneko
Ndikuwoneko
Tiye ponya step (ponya)
Tiye ponya step (ponya)
Tiye ponya step (ponya)
Tiye ponya step (ponya)
Tiye ponya step (ponya)
Tiye ponya step (ponya)
Tiye ponya step (ponya)
Tiye ponya step
Ndilibe jealous, jealous, eh
Ndifuna ndikawoneko ku Nsanje
Zifukwa zoferazi, 'ferazi, eh
Ndikawoneko phiri la Mulanje, yeah
Tikadyeko ma papaya, yeah
Thyolo, Zomba mpaka Blantyre, yeah
Chikwawa nde tansiya, yeah
Tikafika Dedza tikathyole dance ah-huh (eh)
Kungofika ndiku Lilongwe (ah-huh)
Malawi ndikuwala mbe (ah-huh)
Salima mpakana ku Nkhatabay
Tikafika ku Likoma kumakhala phe
Ku Nkhotakota, eh, tikayipota, eh
Nde ku Chitipa, kapesa tikasipa, eh
Malawi
Ndikuwoneko
Ndikuwoneko (mm, hmm)
Malawi
Ndikuwoneko
Ndikuwoneko
Tiye ponya step (ponya)
Tiye ponya step (ponya)
Tiye ponya step (ponya)
Tiye ponya step (ponya)
Tiye ponya step (ponya)
Tiye ponya step (ponya)
Tiye ponya step (ponya)
Tiye ponya step
Mzuzu, Mzimba
Wanakazi wanikhumba
Sound yane wayikhumba
Wayiphulikira umu gumbagumba
My phone is ringing
Kuli nkaka ndi uchi ku Nchinji
Kasungu I be trappin'
I be moving around I ain't stopping'
Tikafike nde ku Dowa
Kumadisi ku Mangochi ndakusowa
Balaka ndikulowa, potuluka Chaku Mwanza ndikudzera
Warm heart of Africa, ask around it is Malawi
Chiradzulu tikafika, atate tipatseni nthawi
Malawi I love you
You're the reason I can put a tattoo, yeah
Uku ndi kwathu
Kukunyadira, that is what what I do, yeah
Malawi
Ndikuwoneko
Ndikuwoneko (mm, hmm)
Malawi
Ndikuwoneko
Ndikuwoneko
Tiye ponya step (ponya)
Tiye ponya step (ponya)
Tiye ponya step (ponya)
Tiye ponya step (ponya)
Tiye ponya step (ponya)
Tiye ponya step (ponya)
Tiye ponya step (ponya)
Tiye ponya step (Loyal- loyal hustle the factory)
04deLyrics