![ZiKaLoWa](https://source.boomplaymusic.com/group10/M00/01/14/1eee1cdccbbb46dbaaf97504cd4dad1eH3000W3000_464_464.jpg)
ZiKaLoWa Lyrics
- Genre:Others
- Year of Release:2025
Lyrics
Imvani Ka nkhani
Kamafana ophusha ngini level ya ntown
Timathamangitsa dzuwa mpaka sundown
Sitigiva sitigonja cha ma round one
Maso pa vision
Ngati waupeza mgodi vunga mission
Timatipula limodzi no collision
Mpaka tizasamukile M'ma location
Kutsogoza Jehova yaaa
Aziyipatsa mofayayayaa
Ku Hasa osatopa yaaaa
Kugona kukamacha timabwerera konko
Kumatsogoza Jehova yaaa
Aziyipatsa mofayayayaa
Ku Hasa osatopa yaaaa
Kugona kukamacha timabwerera konko
Ndani samafuna kukhala happy
Kumasaka dollar nkupanga Money
Ndani samafuna kukhala happy
Kumasaka dollar nkupanga Money
Ah aseee
Tizapuma zikalowa
Ah ase
Tizapuma zikalowa
Yah man yah
Ah aseee
Tizapuma zikalowa
Ah ase
Tizapuma zikalowa
Nde Imva young man
Hustle sikutolatola panga reason
Osamayishosha khoba Kuli prison
Ungazasiye abale Ali nchisoni yayaya
A Chemwa Imvani
Osatengeka ndi dollar za ma big man
Geni sapanga ndi thupi tazisungani
Penapake zikathina ingolimbani yayaya
Kutsogoza Jehova yaaa
Aziyipatsa mofayayayaa
Ku Hasa osatopa yaaaa
Kugona kukamacha timabwerera konko
Kumatsogoza Jehova yaaa
Aziyipatsa mofayayayaa
Ku Hasa osatopa yaaaa
Kugona kukamacha timabwerera konko
Ndani samafuna kukhala happy
Kumasaka dollar nkupanga Money
Ndani samafuna kukhala happy
Kumasaka dollar nkupanga Money
Ah aseee
Tizapuma zikalowa
Ah ase
Tizapuma zikalowa
Yah man yah
Ah aseee
Tizapuma zikalowa
Ah ase
Tizapuma zikalowa